score
float32
1.04
1.25
Chichewa
stringlengths
9
500
Xhosa
stringlengths
9
500
1.241936
Chinthu chilichonse chimene mudzapempha m'mapemphero anu, mudzalandira ngati muli ndi chikhulupiriro."
Kwaye nantoni na oyicelayo ngomthandazo, ukholwa, uya kuyifumana.
1.241869
Kodi kuuka kwa Yesu kunali kosiyana bwanji ndi kuuka kwa anthu ena m'mbuyomo?
Uvuko lukaYesu lwalahluke njani kuvuko lwabantu bangaphambi kwakhe?
1.241857
Koma anthu a mumzindawu anapitirizabe kuchita zoipa.
Sekunjalo, abantu beso sixeko baqhubeka nobubi babo.
1.241761
Ndipo cinatsegula pakamwa pace kukanena zamwano pa Mulungu, kucitira mwano dzina lace, ndi cihema cace, ndi iwo akukhala m'Mwamba.
Lawuvulela umlomo walo ekumnyeliseni uThixo, ukuba lilinyelise igama lakhe, nomnquba wakhe, nabo bahleli emazulwini.
1.241754
Iwo anauzidwa kuti: "Mitundu yonse ya anthu padziko lapansi adzaona kuti mukutchedwa ndi dzina la Yehova, ndipo adzachita nanu mantha."
Axelelwa oku: "Ziya kubona zonke izizwana zomhlaba ukuba igama likaYehova libizwe phezu kwakho, zikoyike."
1.241719
Mulungu amalonjeza anthu amene 'amaganizira za dzina lake' kuti: "Ndidzawachitira chifundo monga mmene munthu amachitira chifundo mwana wake amene amamutumikira."
UThixo uthembisa abo "bacinga ngegama lakhe" esithi: "Ndiza kubabonisa imfesane, kanye njengomntu obonisa imfesane kunyana wakhe omkhonzayo."
1.241701
Ukadzatuluka udzakhala wokalamba komanso wekhawekha."
Uya kuthi uphuma, ube ulixhegokazi elingenabani."
1.241693
18 Tonse tikhoza kutsatira mfundo ya m'mawu a Paulowa.
18 Sonke sinokufunda nto kula mazwi kaPawulos.
1.241671
Mawu Ake amatilimbikitsa 'kumufufuza ndi kumupeza, ngakhale sakhala patali ndi yense wa ife.'
ILizwi lakhe lisikhuthaza ukuba 'simphuthaphuthe size ngokwenene simfumane, nangona, enyanisweni, engekude kuye ngamnye wethu.'
1.241598
Popeza kuti saganiza bwino, zimawavuta kuti asiyanitse choyenera ndi chosayenera.
Xa amandla abo okucinga engasebenzi kakuhle, kuba nzima ukuba bahlule okulungeleyo kokubi.
1.241534
Ndipo iwo anapita kukamenyana ndi ana a Amoni.
Baphuma baya koonyana baka-Amon.
1.241532
"Wandipeza kodi mdani wanga?"
'Undifumene, lutshaba lwam!'
1.241502
Koma musaiwale kucitira cokoma ndi kugawira ena; pakuti nsembe zotere Mulunguakondweranazo.
ke ukwenza okuhle nobudlelane, musani ukukulibala; kuba imibingelelo enjalo uyakholiswa kakuhle yiyo uthixo.
1.241493
Kodi iweyo unayamba wanama? - * Ngakhale akuluakulu ena amene amakonda Mulungu ananamapo.
Ngaba wakha waxoka? - *Nkqu nabantu abadala abamthandayo uThixo bakha baxoka.
1.24149
Palibe tsiku kapena malire a kutsitsa,
Akukho mhla kwaye akukho mda umda ekukhupheleni,
1.241469
Zoyipa zonsezi zimatuluka mʼkati ndipo zimadetsa munthu."
Zonke ezi zinto zingendawo ziphuma ngaphakathi, zimenze inqambi umntu.
1.241465
Yesu anawawuza kuti, "Atate anga amagwira ntchito nthawi zonse mpaka lero lino, ndipo Inenso ndili pa ntchito."
Wawaphendula ke uYesu wathi, UBawo uyasebenza kude kube ngoku, nam ndiyasebenza.
1.24146
"Gula Choonadi Ndipo Usachigulitse"
"Thenga Inyaniso, Ungathengisi Ngayo"
1.241443
Ndipo mudziwa kuti Iyeyu anaonekera kudzachotsa machimo; ndipo mwa Iye mulibe tchimo.
Senazi ukuthi yena wabonakaliswa, ukuze asuse izono; akukho sono kuye.
1.241439
Pakuti ngakhale Khristu sanadzikondweretse yekha."
Kuba kwanoKristu akazange azikholise yena ngokwakhe."
1.241423
Kodi umadziŵa kuti nyenyezi zonse zili ndi mayina awo?
Ngaba ubusazi ukuba zonke iinkwenkwezi zinamagama?
1.241413
Iye anakopa Ayuda ambiri komanso anthu a mitundu ina.
Watsalela kuye inkitha yamaYuda neeNtlanga.
1.241374
Kodi kuuka kwa Yesu kunali kosiyana bwanji ndi kuuka kwa anthu ena m'mbuyomo?
Uvuko lukaYesu lwalahluke njani kolwabantu ababevuswe ngaphambi kwakhe?
1.241363
Thangwi yanji tisafunika kukumbuka nkazi wa Loti?
Kutheni sifanele sikhumbule umkaLote?
1.241328
6 Ifenso tikapirira tidzalandira mphoto.
6 Ukuba siyanyamezela, siya kufumana umvuzo.
1.241248
23 Atate wathu amafuna kuti tiyandikane naye.
23 UBawo wethu ufuna sisondele kuye.
1.24122
Rom 4:15 Pakuti chilamulo chichitira mkwiyo; koma pamene palibe lamulo pamenepo palibe kulakwa,
Ingqumbo kaThixo kaloku ibangwa kukwaphulwa komthetho wakhe; kodwa apho ungekhoyo umthetho akukho kwaphulwa kwamthetho.
1.241198
Baibulo limati: "Awiri aposa mmodzi; pakuti ali ndi mphotho yabwino m'ntchito zawo.
"Ababini balunge ngakumbi kunomnye, ngenxa yokuba banomvuzo ngomsebenzi wabo onzima.
1.241196
Nʼchifukwa chiyani ena a inu mukuganiza kuti nʼkosatheka kuti Mulungu aukitse akufa?
Yini na ukuba nithi, yinto eningenakukholwa yiyo, ukuba uThixo uyabavusa abafileyo?
1.241065
Kodi Mulungu amafuna kuti tizikondwerera masiku amene tinabadwa? -
Ngaba uThixo ufuna sibhiyozele imihla yokuzalwa? -
1.241014
'Ndodo yake yachifumu ndi ndodo yachilungamo' choncho n'zosachita kufunsa kuti iye ndi wolamulira wachilungamo komanso wosakondera.
'Intonga yobukhosi yobukumkani bakhe yintonga yobukhosi yokuthe tye,' ukuqinisekisa ukuba ulawula ngobulungisa yaye akakhethi buso.
1.241
Koma kodi mukudziwa kuti timaphunziranso Baibulo ndi anthu padziko lonse?
Kodwa ubusazi na ukuba sikwafundisa abantu iBhayibhile emhlabeni wonke?
1.240959
Kuopa Mulungu ndiko maziko a nzeru zenizeni.
Ukoyika uThixo kusisiseko sobulumko bokwenyaniso.
1.240957
Cotero munthu ali yense wa ife adzadziwerengera mlandu wace kwa Mulungu.
Ngoko ke elowo kuthi uya kuziphendulela kuThixo.
1.240957
Cotero munthu ali yense wa ife adzadziwerengera mlandu wace kwa Mulungu.
ngoko ke elowo kuthi uya kuziphendulela kuthixo.
1.240931
Iye ndi bwenzi loposa onse.
Ngoyena mhlobo ulungileyo.
1.240928
Ndipo mkaziyo unamuona, ndiye mudzi waukuru, wakucita ufumu pa mafumu a dziko.
Inkazana owayibonayo nguloo mzi mkhulu, ulawula ookumkani bomhlaba.
1.240903
Kodi ndikhoza kukhumudwitsa ena?'
Ngaba andiyi kubakhubekisa abanye?'
1.240828
30Ndipo mumati, 'Ngati tikanakhala mʼmasiku a makolo athu sitikanakhetsa nawo magazi a aneneri.' 31Potero mukutsimikiza kuti muli ana a iwo amene anapha aneneri.
Nithi: 'Ukuba sasikho thina kwimihla yoobawo, ngesingahambisananga nabo ngokubulawa kwabashumayeli.'
1.240798
Iye anati: "Sindine woposa makolo anga."
Wathi: "Andilunganga ngaphezu kookhokho bam."
1.240794
17 Ananso ayenera kukhala odekha.
17 Nabo abantwana kufuneka bazole.
1.240761
iwo anaona ophunzira ake akudya chakudya ndi mʼmanja mwakuda kapena kuti mʼmanja mosasamba.
bathi, bakubona abathile kubafundi bakhe besidla isonka ngezandla eziziinqambi, oko kukuthi ngezingahlanjwanga, basuka basola.
1.240678
Munthu amene akuyenda alibe ulamuliro wowongolera mapazi ake."
Asikokomntu ohambayo ukwalathisa inyathelo lakhe."
1.240653
Tikukupatsani mafungulo onse.
Sikunika zonke izitshixo.
1.240613
Ndingakonde kukusonyeza dzinali m'Baibulo."
Ndithand' ukukubonis' eBhayibhileni."
1.240564
20 Kodi tingakhale tani na cikhulupiro ninga ca Djobi?
20 Singaba nalo njani ukholo olufana nolukaYobhi?
1.240528
Kunena zoona, adani a munthu adzakhala a m'banja lake lenileni."
Eneneni, iintshaba zomntu ziya kuba ngabantu bendlu yakhe."
1.240471
Koma iye amene anali wa mkazi waufulu anabadwa mwa lonjezo.
Ke yena lowo womfazi okhululekileyo wayezelwe ngalo idinga.
1.240408
Tsiku limenelo atumwiwo ananena kuti: "N'zoonadi, Ambuye wauka kwa akufa ndipo waonekera kwa Simoni!"
Abapostile bathi ngaloo mini: "Enyanisweni iNkosi ivusiwe yaye ibonakele kuSimon!"
1.2404
Kodi bambo adakali moyo?'
Utata usaphila kodwa?'
1.240397
12 N'kutheka kuti izi n'zimene zinachitikira Akhristu ena a ku Tesalonika.
12 Kusenokuba kwenzeka ezo zinto kanye kwabathile baseTesalonika.
1.240382
Ndiye Yosefe anawakhululukira.
Ngoko uYosefu wabaxolela.
1.240329
ndi kukhala naco cikhulupiriro ndi cikumbu mtima cokoma, cimene ena adacikankha, cikhulupiriro cao cidatayika;
unokholo nesazela esilungileyo, ethe inxenye, isigibile, yaphukelwa ngumkhombe mayelana nokholo;
1.240283
Koma Mulungu amafuna kuti amene amamulambira azikhulupirira kuti iye alikodi komanso kuti amawakonda.
Kodwa yena ke uThixo ufuna abo bamkhonzayo baqiniseke ukuba ukho yaye uyabathanda.
1.24027
Ndinalibe ndalama zoyendera kupita ku New York.
Ndandingenamali yokuya eNew York.
1.240177
Ulamuliro wake ndiye ulamuliro wamuyaya woti sudzatha, ndi ufumu wake sudzaonongeka. ."
Ulawulo lwakhe lulawulo oluhlala ngokungenammiselo olungayi kudlula, nobukumkani bakhe bobungayi konakaliswa."
1.240082
(Juwau 8:44) Iye adakhala nyamagunkha ndipo adapandukira Mulungu.
(Yohane 8:44) Waba lixoki elavukela uThixo.
1.240032
Munthu akagwiritsitsa nzeru, zidzakhala ngati mtengo wa moyo kwa iye, ndipo ozigwiritsitsa adzatchedwa odala."
Bungumthi wobomi kwabo babubambayo, nabo babubamba nkqi kuya kuthiwa banoyolo."
1.240017
Anapulumutsidwa "Pamodzi ndi Anthu Ena 7"
Wasindiswa "Nabanye Abasixhenxe"
1.240011
Kodi kalata ya Yohane ingatithandize bwanji pa nkhaniyi?
Incwadi kaYohane inokusinceda njani senze loo nto?
1.239959
chifukwa aliyense amene anafa anamasuka ku tchimo.
ngokuba ofileyo ukhululiwe esonweni.
1.239896
Kodi sindine mtumwi?
Andinguye na andimpostile?
1.239886
Mʼmalo mwake tsono, muyenera kumukhululukira ndi kumulimbikitsa mtima kuti asamve chisoni choposa muyeso, angataye mtima.
ngokokude nithi kanye senimxolela, nimthuthuzele, hleze lowo unjalo aselesuka edliwa kukuba buhlungu ngokugqithiseleyo.
1.239873
Olalikira ndi zolinga zabwinowa amachita izi mwachikondi, podziwa kuti ine ndili muno chifukwa cha kuteteza Uthenga Wabwino.
Abo ke baqhutywa luthando, kuba bayazi ukuba uThixo undiphathise umsebenzi wokukhusela udaba olungoKrestu.
1.239873
ndipo sanamdziwe iye kufikira atabala mwana wake; namutcha dzina lake Yesu.
waza ke akamazi, wada wazala unyana wakhe wamazibulo; wambiza ke ngegama elinguYesu.
1.239822
Ndipo pamene mupemphera musabwebwe zambiri, monga akunja; chifukwa akuganiza kuti adzamveka ngati alankhula mawu ambiri.
Ke xa nithandazayo ze ningenzi milembelele ingento njengabangakholwayo, bona baba boviwa ngenxa yamazwi abo amaninzi.
1.239818
amene makolo athu sanafuna kumvera iye, koma anamkankha acoke, nabwerera m'mbuyo mumtima mwao ku Aigupto,
abangathandanga kumlulamela oobawo bethu, besuka bamgiba, babuyela eYiputa ngeentliziyo zabo,
1.239816
Kenako anauza Yosefe kuti: "Popeza kuti Mulungu wakudziwitsa zonsezi, palibenso munthu wina wozindikira ndi wanzeru ngati iwe.
KuYosefu wathi: "Ekubeni uThixo ekwazisile konke oku, akukho bani uyingqondi nosisilumko njengawe.
1.239812
Iwo ankachita zonse zimene angathe kuti andifike pamtima.
Bazama yonke into ukuze bafikelele intliziyo yam.
1.239803
"Musamakhulupirire anthu olemekezeka, kapena mwana wa munthu wina aliyense wochokera kufumbi amene alibe chipulumutso.
"Musani ukukholosa ngamanene, ngonyana womntu, yena ungenalo usindiso.
1.239771
Anthu amene ali m'gulu la kapolo wokhulupirikayu adzapatsidwa udindowu pamene adzalandira mphoto yawo yolamulira limodzi ndi Khristu kumwamba.
Abo babumba eli khoboka lithembekileyo baya kumiselwa xa befumana umvuzo wokuphila ezulwini, balawule kunye noKristu.
1.239761
Popeza Mulungu ndi wamuyaya, zaka 1,000 zili ngati tsiku limodzi kwa iye.
Ekubeni enguThixo kanaphakade, iminyaka eliwaka kuye ifana nosuku.
1.239761
"Iye Sali Kutali ndi Aliyense wa Ife"
'Akakho kude kuye ngamnye wethu.'
1.239742
Ndipo ananena kwa ine, Tapenya, usachite; ndine kapolo mnzako, ndi mnzao wa abale ako aneneri, ndi wa iwo akusunga mau a buku ili; lambira Mulungu.
Sithi kum, Lumka, ungenjenjalo; kuba ndingumkhonzi kunye nawe, nabazalwana bakho abaprofeti, nabo bawagcinayo amazwi ale ncwadi; qubuda kuThixo.
1.239739
Muzifunafuna Ufumu Osati Zinthu Zina
Funa UBukumkani, Kungekhona Izinto
1.239732
Pakuti iye analamula ndipo zinalengedwa.+
Kuba yena wayalela, zona zadalwa.+
1.239707
amene makolo athu sanafuna kumvera iye, koma anamkankha achoke, nabwerera m'mbuyo mumtima mwao ku Ejipito,
abangathandanga kumlulamela oobawo bethu, besuka bamgiba, babuyela eYiputa ngeentliziyo zabo,
1.239704
Nthaŵi zonse Mulungu wathu sadzataya amene ali okhulupirika kwa iye.
UThixo wethu akasayi kuze nanini na abashiye abo banyanisekileyo kuye.
1.239698
Pakuti chilengedwe chikudikira ndi chiyembekezo kuonetsedwa poyera kwa ana a Mulungu.
Kuba indalo ilinde ngolangazelelo olukhulu ukutyhilwa koonyana bakaThixo.
1.239691
Kodi mutha kupulumuka sabata yatha?
Ngaba ungasinda kwiveki ephelileyo?
1.239664
Ndiye dzifunseni kuti, 'Kodi n'kutheka kuti Mulungu akugwiritsa ntchito anthu amenewa pofuna kundikokera kwa iye?'
Khawuzibuze, 'Ngaba mhlawumbi uThixo usebenzisa wona ukuze afike nakum?'
1.239633
Tsono pomwe idafika nthawe ya bzisapo, iye adatumiza kapolo wace kwa alimiwo kuti akatambire bzisapo bzinango bza m'munda wa mpesayo.
Ngexesha lokuvuthwa kweziqhamo ke, wathumela isicaka kubaqeshi, ukuze bamnike imali yengqesho.
1.239624
Kodi n'cifunilo ca Mulungu kuti ife anthu tizifa?
Ngaba ukufa kukuthanda kukaThixo ngoluntu?
1.239605
Mose sanathe kuona Mulungu, koma anamva mawu a Mulungu.
UMoses wayengenakumbona uThixo, kodwa waliva ilizwi likaThixo.
1.239596
Nikodemo ananena kwa Iye, Munthu akhoza bwanji kubadwa atakalamba?
Uthi uNikodemo kuye, Angathini na umntu ukuzalwa emdala?
1.239578
Koma ndikuwuzani kuti musalumbire ndi pangʼono pomwe kutchula kumwamba chifukwa kuli mpando waufumu wa Mulungu.
Ke mna ndithi kuni, Maningakhe nifunge nto; nokuba lizulu,ngokuba yitrone kaThixo;
1.239568
Pakuti ayenera kuchita ufumu kufikira [Mulungu] ataika adani onse pansi pa mapazi ake.
Kuba umelwe yena kukuthi alawule, ade azibeke phantsi kweenyawo zakhe zonke iintshaba.
1.239542
"Palibenso Thanthwe Longa Mulungu Wathu"
"Akukho Liwa LinjengoThixo Wethu"
1.23953
Mbwenye Salomoni amanga banja na akazi azinji a madziko anango, akuti akhalambira madzimunthu.
Kodwa uSolomon watshata abafazi abaninzi ababehlala kwamanye amazwe, ibe aba bafazi babenqula izithixo.
1.239517
Koma ayamikidwe Mulungu, kuti ngakhale mudakhala akapolo a uchimo, tsopano mwamvera ndi mtima makhalidwe aja a chiphunzitso chimene munaperekedweracho;
Ke kaloku, makubulelwe kuThixo, kuba nanifudula nilawulwa sisono, kodwa ngoku niyithobela ngokupheleleyo imfundiso eniyifundisiweyo.
1.239504
Kodi Yesu ankatanthauza chiyani pamene anati: "Iwe udzakhala nane m'Paradaiso"?
Wayethetha ukuthini uYesu xa wathi: "Uya kuba nam eParadesi"?
1.239502
Matauni 5 ku France komwe mungakonde kukhala
Iidolophu ezi-5 eFrance apho ungathanda ukuhlala khona
1.239477
Ndipo pamene mupemphera musabwebwe zambiri, monga akunja; chifukwa akuganiza kuti adzamveka ngati alankhula mawu ambiri.
Nithandaza njalo ke, maningenzi milembelele ingeyanto,njengabeentlanga; kuba beba boviwa ngenxa yamazwi abo amaninzi.
1.239455
Koma pamenepo ine ndidzawauza mwachimvekere kuti: Sindinakudziweni konse chiyambire!
Ukanti ndiya kwandula ndivume kubo ndithi: Andizange ndinazi!
1.239448
Ine ndi Atate ndife amodzi.
Mna noBawo simnye. "
1.239447
Anthu osaona ndi olumala anabwera kwa Iye mʼNyumba ya Mulungu ndipo anawachiritsa.
Kweza kuye iimfama neziqhwala, etempileni apho, waziphilisa.
1.239427
Koma tsono musakondwere kwambiri kuti mizimu inakugonjerani, koma kuti mukondwere ngati mayina anu alembedwa m'mwamba.
Noko ke maningakuvuyeli oku, kokuba oomoya benithobele; vuyelani ke kanye okokuba amagama enu ebhaliwe emazulwini.
1.239396
Ndipo iwo anaponyera fumbi pamitu pawo, nafuwula, akulira, ndi kulira, nanena, Tsoka, tsoka, mudzi waukulu, m'mene onse okhala nazo zombo m'nyanja analemera ndi cuma cace; pakuti iye anawonongedwa mu ora limodzi.
Bagalela uthuli entloko, Bamana bedanduluka, belila,besenza isijwili, Besithi, Yeha, yeha, mzimkhulu, Apho baba nobutyebi khona bonke aba baneenqanawa elwandle, ngeento ezinqabileyo zawo!
1.239266
Abale athu amatisamalira bwino tsiku ndi tsiku.
Abazalwana basinyamekela yonke imihla.
1.239226
Kenako iye sanaonekenso, chifukwa Mulungu anam'tenga."
Wandula ke wanyamalala, kuba uThixo wamthabatha."