score
float32
1.04
1.25
Chichewa
stringlengths
9
500
Xhosa
stringlengths
9
500
1.236894
12 Pemphero ndi lothandiza kwambiri chifukwa Mulungu amamva mapemphero athu.
12 Umthandazo yeyona ndlela uThixo anokusinceda ngayo.
1.236885
koma aliyense adzachitira Mzimu Woyera mwano alibe kukhululukidwa nthawi yonse, koma anapalamuladi tchimo losatha;
kodwa yena othe wanyelisa uMoya oyiNgcwele akanako ukuxolelwa naphakade; unetyala lesono esingatshitshiyo."
1.236875
Taonani ena mwa madalitso amene anthu amenewa adzasangalale nawo mu Ufumu wa Mulungu.
Makhe sithethe ngezinye zeentsikelelo abaya kuzifumana kuBukumkani bukaThixo.
1.236783
Ndipo iwowa adzachotsedwa kwamuyaya, koma olungama kumoyo wosatha. "
46 Baya kumka aba baye elubethweni olungunaphakade; ke wona amalungisa aya kuya ebomini obungunaphakade. "
1.236775
32 Mbwenye Ine ndingadza kathukulwa pantsi pano, ndinacita kuti anthu onsene akundike adze kuna Ine." 33 Yezu alonga penepi, akhafuna pangisa mafero akhafuna cita Iye.
32 Mna ke, ukuba ndithe ndaphakanyiswa emhlabeni, ndiya kubatsalela bonke kum.
1.236771
"Simukudziwa Tsiku Kapena Ola Lake"
'Aniyazi Imini Okanye Ilixa'
1.236762
ndipo sanamdziwe iye kufikira atabala mwana wake; namutcha dzina lake Yesu.
waza ke akamazi, wada wazala unyana wakhe wamazibulo;wambiza ke ngegama elinguYesu.
1.236753
Paulo anaphunzira kutumikira Mulungu popanda kunong'oneza bondo
UPawulos wafunda ukukhonza uThixo ngaphandle kokuzisola
1.236717
Iye analenga anthu m'njira yoti azisangalala akamamudziwa bwino komanso kumutumikira mokhulupirika.
Wadala abantu ngohlobo lokuba kufuneke bamazi kwaye bamkhonze ngokuthembeka ukuze bonwabe.
1.236714
Aliyense ayenera kunyamula katundu wake. - Agal.
Ngamnye uya kuthwala owakhe umthwalo. - Gal.
1.236701
Kodi Mulungu anatilenga anthufe ndi maganizo ofuna kuchita zoipa?
Ngaba uThixo wabadala abantu baneengcinga ezimbi?
1.236653
Koma tikhulupira tidzapulumuka mwa cisomo ca Ambuye Yesu Kristu, monga iwo omwe.
Ke ngalo ubabalo lweNkosi uYesu Kristu, siyakholwa ukuba sosindiswa kwangohlobo ezisindiswa ngalo nazo.
1.236628
Kodi Mulungu adzawononga bwanji adani onsewa?
UThixo uza kuzitshitshisa njani ezi zinto ziziintshaba?
1.236571
9 Kodi mungafune kuthandiza apainiya mu utumiki?
9 Ngaba ungathanda ukuncedisa oovulindlela entsimini?
1.23657
Koma aliyense m'magawo ake: Kristu chipatso choyambirira, pambuyo pake iwo a Khristu nthawi ya kukhalapo kwake.
Kodwa ngamnye kuluhlu lwakhe: UKristu intlahlela, emva koko abo bangabakaKristu [abaza kulawula naye] ebudeni bobukho bakhe.
1.236551
Koma cakudya sicitibvomerezetsa kwa Mulungu; kapena ngati sitidya sitisowa; kapena ngati tidya tiribe kupindulako,
Ukudla akusithandisi kuye uThixo; kuba nokuba sithe sadla, asigqithe nganto; nokuba asithanga sidle, asisilele nganto.
1.236509
Russian ndi Germany: ndani amapambana?
IsiRashiya nesiJamani: ngubani ophumeleleyo?
1.236488
Ndiye olungama adzasonkhanitsa za ine chifukwa cha ubwino wanu kwa ine.
Aya kwandula ke amalungisa ndawonye ngam ngenxa yokulunga kwakho kum.
1.236486
Oipa akadzadulidwa, iwe udzaona. "
Xa abangendawo benqunyulwa, uya kubona."
1.2364
Iye anaphunzira zinthu zambiri kwa Atate wake ndipo ankaziyamikira kwambiri.
Wafund' into eninzi gqitha kuYise, ibe wayezixabisa nyhani izinto awazifundayo.
1.236392
ndipo lidafa limodzi la magawo atatu a zolengedwa zili m'nyanja, zokhala ndi moyo; ndipo limodzi la magawo atatu a zombo lidaonongeka.
safa isahlulo sesithathu sezidalwa eziphilileyo eziselwandle; nesahlulo sesithathu semikhombe sonakaliswa.
1.23639
Luk 21:29 Ndipo adanena nawo fanizo; Onani mtengo wa mkuyu ndi mitengo yonse;
21:29 Wathetha umzekeliso kubo, wathi, Wukhangeleni umkhiwane nemithi yonke;
1.236386
Kodi ndi tsiku lina liti lachiweruzo limene lidzabweretsa madalitso kwa anthu?
Yiyiphi enye imini yomgwebo eza kunceda abantu?
1.236385
Pamene unyinji wa nyanja adzakhala anatembenukira kwa inu, mphamvu ya mitundu ya anthu zikakupezani.
Xa intabalala yolwandle iya sele iguqulelwe kuwe, uya amandla kweentlanga kuwe.
1.236382
Nsiku iri-yense imbakwane na bzakuipa bzace.'
Imini nganye inobayo ububi obuyilingeneyo.'
1.236331
Mkaziyo adati: 'Mbuya, ndipaseni madziyo!
'Nkosi,' utsho lo mfazi, 'ndiphe loo manzi!
1.236323
Mulungu analenga "mwamuna ndi mkazi" ndipo anaona kuti zonse zimene analenga zinali "zabwino kwambiri."
UThixo wadala "indoda nebhinqa" waza wabona ukuba konke akwenzileyo 'kulunge gqitha.'
1.236296
Komabe, iwo anali asanasonyezebe chikhulupiriro chilichonse.
Noko ke, babengekabi nalo ukholo.
1.236271
Kuti tidziwe zimenezi, tiye tikambirane kaye zimene zinachitika Mariya asanakwatiwe.
Ukuze sibone oku, masiqale sibone oko kwenzekayo ngaphambi kokuba uMariya atshate.
1.236232
Kodi ukuganiza kuti mnyamatayu ayenera kuti anali ndani? - Ayenera kuti anali Maliko amene.
Ucinga ukuba yayingubani lo mfana? - Ewe, mhlawumbi yayinguMarko!
1.236226
Komabe nditachotsa mimba ndinkamva kuti ndachita zinthu zoipa kwambiri." * Koma kodi Mulungu sangamukhululukire chifukwa cha zimene anachitazi?
Kodwa emva kokuba ndikhuphe isisu, ndaziva ukuba ndenze eyona nto yakha yambi." * Ngaba wayenze into uThixo awayengenakumxolela ngayo?
1.236192
Zimenezi zimandichititsa kukhala ndi mtima wofuna kupitiriza kulalikira."
Kundenza ndihlale ndifuna ukushumayela."
1.236183
Ndipo ife ndife mboni za zinthu izi; Mzimu Woyeranso, amene Mulungu anapatsa kwa iwo akumvera iye.
"Kwaye singamangqina ezi zinto, kwaye kunjalo UMoya oyiNgcwele, athe uThixo wabanika abo bamthobelayo. "
1.236171
Tidziwa kuti yense wobadwa kuchokera mwa Mulungu sachimwa, koma iye wobadwa kuchokera mwa Mulungu adzisunga yekha, ndipo woipayo samkhudza.
Siyazi ukuba bonke abazelwe nguThixo aboni;
1.236171
Koma kodi Yohane ndi Yesu akuchitanji tsopano?
Kodwa uYohane noYesu benza ntoni ngoku?
1.236124
Yankho la Stephan ..."Osati motalika kwambiri.
Mpendulo kaStephan ..."Kungekude kakhulu.
1.23605
Ndipo wokhala pampando wachifumu anati: 'Taonani!
Waza Lowo uhleli etroneni wathi: 'Khangela!
1.236037
Koma miyamba ndi dziko lapansi kuti tsopano alipo ndi mawu omwewo anapulumutsa moto ndipo anasunga mpaka tsiku pamene anthu osapembedza adzaweruzidwa ndi kuwonongedwa. "
Ke lona izulu langoku, nawo umhlaba lo, kwangelo lizwi ezo zinto ziqwetyelwe, zigcinelwe, umlilo, kuse kwimini yomgwebo nentshabalalo yabantu abangahloneli Thixo.
1.235978
Iye anati: "Mtengo wabwino uliwonse upatsa zipatso zokoma; koma mtengo wamphuchi upatsa zipatso zoipa.
Wathi: "Wonke umthi olungileyo uvelisa iziqhamo ezihle, kodwa wona umthi ongalunganga uvelisa iziqhamo ezibi.
1.23595
Ndiponso, 'Ngati munthu akalumbira kutchula guwa lansembe, palibe kanthu; koma amene akalumbira kutchula mphatso ya pamwamba pake, walumbira. '
Kanjalo nina nithi, Othe wafunga isibingelelo, akunto oko; ke othe wafunga umnikelo ophezu kwaso, unetyala.
1.235921
Citani khama m'kupemphera, nimudikire momwemo ndi ciyamiko;
Qiniselani ekukhulekeni, nilinde kukho ninokubonga.
1.235877
Koma tikhulupira tidzapulumuka mwa cisomo ca Ambuye Yesu Kristu, monga iwo omwe.
Ke thina siyakholwa ukuba sosindiswa ngalo ubabalo lweNkosi uYesu, kwangokunjalo baya kusindiswa ngabo.
1.235865
Mutha kumapemphera onse, koma osati tsiku lomwelo.
Unokuthandaza nonke, kodwa hayi ngosuku olunye.
1.235849
"Lero sindikumva bwino m'thupi.
"Andiziva mnandi namhlanje.
1.235843
7 M'Baibulo, nthawi zina mapiri amaimira maufumu kapena kuti maboma.
7 EBhayibhileni, ngamanye amaxesha iintaba zimela ookumkani okanye oorhulumente.
1.235842
Kodi Mose anazindikira chiyani zokhudza 'zosangalatsa zauchimo'?
Yintoni awayeyiqonda uMoses 'ngokuziyolisa ngesono'?
1.235792
Yehova ali ndi tonsefe, osati iweyo ndi Aroni basi.'
UYehova akaxhasi wena noAron kuphela, kodwa unathi sonke.'
1.235789
Khalani woyamba ku Turkey ..!
Yiba ngowokuqala eTurkey ..!
1.235764
Kwa $ 80 iyi inali yabwinoko kuposa momwe ndimayembekezera ..
I $ 80 le ibingcono kunokuba bendikade ndikulindele ..
1.235751
Nʼchifukwa chake ngati zimene ine ndimadya zichititsa mʼbale wanga kugwa mu tchimo, sindidzadyanso chakudyacho kuti mʼbaleyo ndisamuchimwitse.
Ngenxa yoko ndithi, Ukuba ukudla kuyamkhubekisa umzalwana wam, andisayi kudla nyama naphakade, ukuze ndingamkhubekisi umzalwana wam.
1.23573
Yesu anafunsa kuti, "Kodi amene anachiritsidwa sanalipo khumi?
Waza uYesu wathi: "Bekungahlanjululwanga balishumi na?
1.235681
16 Kodi mnyamatayo ankamva bwanji?
16 Wavakalelwa njani yena unyana wabo?
1.235608
Ndipo anati kwa iwo, Ndinaona Satana alinkugwa ngati mphezi wochokera kumwamba.
Wathi ke kubo: "Ndibone uSathana esiwa ezulwini okombane.
1.235596
Kumbukilani Mkazi wa Loti
Khumbulani UmkaLote
1.235595
Fotokozani mavuto amene aneneri ena anakumana nawo chifukwa cha chikhulupiriro chawo.
Abanye abaprofeti banyamezela buphi ubunzima ngenxa yokholo lwabo?
1.235589
Kodi zimenezi zikusonyeza kuti anali wochokera ku Girisi?
Ngaba oku kuthetha ukuba wayengowaseGrisi?
1.235558
Heb 9:27 Ndipo monga kwayikikatu kwa anthu kufa kamodzi, ndipo atafa, chiweruziro:
9:27 Ke kwanjengokuba ke abantu bemiselwe ukuba bafe kube kanye, ize ke emveni koko ibe ngumgwebo:
1.235536
Kodi ndi zinthu zina ziti zimene ndikuphunzira pa pemphero limeneli?' - Sal.
Ziziphi izinto endinokuzifunda kulo mthandazo ucingisisiweyo?' - INdu.
1.235522
Ngati mwayambana menyanani nokhanokha ife zisatikhuze.
Ukuba ke niyagrenyana, nidlane, lumkani ukuba ningagqitywa omnye ngomnye.
1.235502
Poyamba, ine ndi M'bale Lennart Johnson tinali ndi ntchito yambiri.
Ekuqaleni, yayindim noLennart Johnson ababesenza umsebenzi omninzi.
1.235495
Chonde timangireni Nyumba ya Ufumu yabwino."
Sicela nisakhele iHolo yoBukumkani entle!"
1.235465
Woyambitsa Ndikufuna Kukhala Blogger / Twitter
UMsunguli Ndifuna ukuba yiBlogger / Twitter
1.235463
Pakuti amene Mulungu anawadziwiratu, anawasankhiratunso kuti akonzedwe mʼchifanizo cha Mwana wake, kuti Iye akhale Mwana woyamba kubadwa mwa abale ambiri.
Kuba abo uThixo ngaphambili babemisele ngaphambili ukuba bafanelane nomfanekiso woNyana wakhe, ukuze abe ngowamazibulo phakathi kwabazalwana noodade abaninzi.
1.235448
Kodi zimene munkadziwa zokhudza sayansi zinapangitsa kuti muvutike kuyamba kukhulupirira Mulungu?
Ngaba ukwazi isayensi kwenze kwanzima ukuba ukholelwe kuThixo?
1.235395
Pakuti chilengedwe chikudikira ndi chiyembekezo kuonetsedwa poyera kwa ana a Mulungu.
Kuba ukulangazelela kwendalo kulinde ukutyhileka koonyana bakaThixo.
1.235395
Ndipo imfa ndi Hade zinaponyedwa m'nyanja yamoto.
Kwaza ukufa nelabafileyo kwaphoswa edikeni lomlilo.
1.235383
Choyamba, ndimamva kuti mukasonkhana mu mpingo, pamakhala magawano pakati panu; ndipo ndimakhulupirira kwambiri. "
Kuba kuqalake, nakuhlangana ebandleni, ndiyeva ukuba kubakho izahlukahlukano phakathi kwenu; ndithi ke kufanele ukuba zikho.
1.235366
M'tsiku limenelo, ziweto zanu zidzadya msipu pamalo aakulu odyetserapo ziweto." - Yes.
Imfuyo yakho iya kudla ngaloo mini kwidlelo eliphangaleleyo." - Isa.
1.235344
Patapita zaka ziwiri, mu 2007, ndinapita m'dziko la Mongolia.
Emva kweminyaka emibini, ngo-2007, ndaya kutyelela eMongolia.
1.23531
Kodi inuyo mumafuna mutadzaonananso ndi ndani, akufa akamadzaukitsidwa?
Ngubani ongathanda ukumbona nakuvuswa abantu?
1.235291
Mose ankadziwa tanthauzo la dzina la Mulungu ndipo zimenezi zinalimbitsa chikhulupiriro chake
Ukwazi intsingiselo yegama likaThixo kwalomeleza ukholo lukaMoses
1.235267
Mose sanachite mantha ndi zimene Farao angachite atamva zimenezi.
UMoses wayengoyiki.
1.235262
Kodi si nthawi yoti tiyende?!;)
Ngaba ayilixesha lethu lokuba sihambe?!;)
1.23524
Anawauza kuti: "Nonsenu ndinu abale."
Wathi kubo: "Nonke nina ningabazalwana."
1.235233
Zikuyenera kuti zikhale akapolo.
Kusenokwenzeka ukuba yayizizicaka.
1.235219
Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona."
Xa abangendawo benqunyulwa, uya kubona."
1.235161
Pali zinthu zambiri zimene zimatitsimikizira kuti kuli Mulungu yemwe ndi Mlengi wanzeru, wamphamvu komanso wachikondi.
Inyaniso yeyokuba singqongwe bubungqina bobukho boMdali onobulumko, amandla, nothando.
1.235157
Zimenezi zikutanthauza kuti Yesu ankagwiritsa ntchito dzina la Mulungu momasuka monga ankachitira aneneri onse amene analipo Yesuyo asanadzabadwe.
Ngaloo ndlela uYesu ufanele ukuba wayelisebenzisa ngokukhululekileyo igama likaThixo njengabaprofeti ababengaphambi kwakhe.
1.235155
Kodi ifenso tikhoza kulandira nzeru zochokera kwa Mulungu?
Ngaba nathi sinako ukufumana ubulumko obuvela kuThixo?
1.235141
(Genesis 2:18) Mulungu analenga Adamu ndi Hava monga anthu awiri osiyana koma anali oyenererana.
(Genesis 2:18) UThixo wabadala baneempawu ezahlukeneyo ukuze bangafani, kodwa bafanelane.
1.23513
Mibvunzo: Kodi Danyeri akhacita ciyani katatu pa nsiku?
Imibuzo: Yintoni awayeyenza kathathu ngemini uDaniyeli?
1.235086
Yesu ameneyo, Mulungu anamuukitsa; za ichi tili mboni ife tonse.
UThixo wamvusa lo Yesu, esingamangqina ako oko thina sonke.
1.235073
Iye analemba kuti: "M'masiku amenewo, amuna 10 ochokera m'zilankhulo zonse za anthu a mitundu ina adzagwira chovala cha munthu amene ndi Myuda ndi kunena kuti: 'Anthu inu tipita nanu limodzi, chifukwa tamva kuti Mulungu ali ndi inu.'"
Wathi: "Ngezo mini ke amadoda alishumi aphuma kuzo zonke iilwimi zeentlanga aya kubamba, ewe, okunene aya kubamba isondo lendoda engumYuda, esithi: 'Siza kuhamba nani, kuba sivile ukuba uThixo unani.'"
1.235056
Kodi mumakhala kunja kwa United States?*
Ngaba uhlala ngaphandle kweUnited States?*
1.235034
Koma pamene limayamba kuchitika, ndiye limbitsani tukulani mitu yanu, chifukwa chipulumutso chanu likuyandikira. "
Ke kaloku, zakubon ukuba ezi zinto ziyaqala ukuhla, sukani nime, niziphakamise iintloko zenu, ngenxa yokuba iyasondela inkululeko yenu.
1.234996
Panopa Martín amaona kuti moyo wake ndi waphindu
Ngoku uMartín uphila ubomi obunenjongo
1.234984
Ife tinasiya zinthu zonse ndipo takhala tikukutsatirani."+
Sishiye zonke izinto sakulandela."+
1.234931
6:24 Palibe wina angathe kutumikira ambuye awiri.
6:24 Akukho mntu unako ukukhonza nkosi mbini.
1.23493
Mulungu ali ndi mphamvu komanso nzeru zopanda malire.
UThixo unamandla nobulumko obungenasiphelo.
1.234909
Paulo anaphunzira kutumikira Mulungu popanda kunong'oneza bondo
UPowula wafunda indlela yokukhonza ngaphandle kokuzisola
1.234897
Koma Yesu anati, "Wina wandikhudza; ndikudziwa chifukwa mphamvu yachoka mwa Ine."
Uthe ke uYesu, Ukho ondichukumisileyo; kuba mna ndiyawazi amandla aphumileyo kum.
1.234896
"Katsala kanthawi ndipo woipa adzatha psiti: Inde, udzayang'anira mbuto yake, nudzapeza palibe.
"Sekusele ithutyana, bangabikho abenzi-bubi; Xa ujonga apho bebekho, Baza kube bengasekho.
1.234844
Iye anauza atumwi ake okhulupirika kuti: "Mupitiriza kukhala mabwenzi anga mukamachita zimene ndikukulamulani."
UYesu wathi kubapostile bakhe: "Ningabahlobo bam ukuba nenza oko ndiniyalela kona."
1.234769
Koma popeza Mulungu ndi wosaoneka, kodi 'tingamuyandikire' bwanji n'kukhala mnzathu wapamtima?
Kodwa ke, ekubeni uThixo engabonakali 'ungasondela' njani kuye uze ube ngumhlobo wakhe?
1.234748
Koma nʼchifukwa chiyani andikomera mtima kuti amayi a Ambuye anga abwere kwa ine?
Ndingubani na ukuba ndingade ndihanjelwe ngumama weNkosi yam? ."
1.234735
Ndikuphunzira kukhala nawo ku Neuro. "
Ndifunda ukuhlala kubo eNeuro. "
1.234723
Muyenera kupitiliza kugwira ntchito, ndipo zidzakhala bwino mawa.'
Kufuneka uqhubeke usebenza, kwaye kuya kuba ngcono ngomso.'
1.234702
(Danieli 7:13, 14) Ndipotu lemba la Salimo 72:12, 14 limanena kuti: "[Yesu] adzalanditsa wosauka wofuulira thandizo, komanso wosautsika ndi aliyense wopanda womuthandiza."
(Daniyeli 7:13, 14) INdumiso 72:12, 14 ithi, "[UYesu] uya kumhlangula lowo ulihlwempu ukhalela uncedo, kwanalowo uxhwalekileyo nabani na ongenamncedi.
1.234696
Ndinazindikiranso kuti abale padziko lonse akundipempherera."
Ndandisazi ukuba abazalwana abasehlabathini jikelele babendithandazela."
1.234649
"Kale simunali mtundu, koma tsopano ndinu mtundu wa anthu a Mulungu." - 1 PET.
"Nanikhe anabi sisizwana, kodwa ngoku nisisizwana sikaThixo." - 1 PET.