score
float32
1.04
1.25
Chichewa
stringlengths
9
500
Xhosa
stringlengths
9
500
1.244532
Pamenepo ophunzirawo anati: 'Ambuye, ngati iye akupumula, apeza bwino.'
Ngoko ke abafundi bathi kuye: 'Nkosi, ukuba uye kuphumla, uya kuphila.'
1.24446
1Co 6:8 Koma muyipsa, nimunyenga, ndipo mutero nawo abale anu.
6:8 Ke nina nenza ukuzenzakalisa kunye ukukopela, yaye oku kubo abazalwana!
1.244442
Nthawi zina ndinkamva ngati mneneri Danieli, yemwe atalandira mawu aulosi kuchokera kwa mngelo ananena kuti: "Ndinamva zimene ananenazo, koma sindinadziwe tanthauzo lake."
Ndandifana nomprofeti uDaniyeli, owathi emva kokufumana isiprofeto kwingelosi: "Ndakuva oko, kodwa andakuqonda."
1.244438
Dziko lonse silili pamaso pako kodi?
Aliphambi kwakho na ilizwe lonke?
1.244436
N'chifukwa chiyani Mose ankaona kuti utumiki wake ndi wofunika kwambiri?
Kwakutheni ukuze uMoses asixabise isabelo sakhe?
1.244415
Koma n'zomvetsa chisoni kuti mkazi wanga wokondedwa, Maria, anamwalira mu 2014.
Ngelishwa, inkosikazi yam endiyithanda kunene, uMaria, yasweleka ngo-2014.
1.244402
ndipo sindidzakumbukiranso machimo awo."
kwaye abayi kuphinda bakhumbule izono zabo.
1.244398
Ndipo pamene adakhuta, Iyeananena kwa akuphunzira ace, Sonkhanitsani makombo kuti kasatayike kanthu.
Bakuhlutha ke, uthi kubafundi bakhe, Buthani amaqhekeza aseleyo, ukuze kungonakali nto.
1.244375
44 Koma iwo adaganiza kuti Iye adali m'chipilingu cha ulendo, nayenda ulendo wa tsiku limodzi; ndipo adayamba kumfunafuna Iye mwa abale awo ndi mwa anansi awo.
44 Babeba ke bona usemkhokweni wabahambi, bahamba uhambo lwamini-nye; bamana bemfuna phakathi kwemizalwana, naphakathi kwabazana nabo.
1.244375
Pakuti mau a mtanda ali ndithu cinthu copusa kwa iwo akutayika, koma kwa ife amene tirikupulumutsidwa ali mphamvu ya Mulungu.
Kuba ilizwi lomnqamlezo libubudenge okunene kwabatshabalalayo; kodwa ke kwabasindiswayo, thina aba, lingamandla kaThixo.
1.244374
Mulungu sanalenge anthu kuti azifa, koma kuti azikhala ndi moyo wosatha.
UThixo akazange abadalele ukuba bafe abantu kodwa wayefuna baphile ngonaphakade.
1.244287
kapena ngati munthu waganyu woyembekezera malipiro ake,
Okanye anike uThixo intlawulelo ngaye;
1.244282
Tsiku lililonse, mlongo wanga anabwera.
Yonke imihla, kweza udade wam.
1.244254
Kodi tiyenera kuopa Mulungu chifukwa choti ndi wamphamvu?
Ngaba sifanele simoyike uThixo ngenxa yokuba enamandla?
1.244208
Nanga kodi pali nthawi zina pamene amawachitira chifundo?'
Ngaba kukhe kuthethe izenzo zenceba?'
1.244207
Unakhulupirika pa zinthu zochepa.
Ubuthembekile kwizinto ezimbalwa.
1.244185
Tsopano muyenera kumukhululukira ndi kumtonthoza, kuti asataye mtima ndi chisoni chochuluka.
ngokokude nithi kanye senimxolela, nimthuthuzele, hleze lowo unjalo aselesuka edliwa kukuba buhlungu ngokugqithiseleyo.
1.244131
Kodi kupha nyama n'kulakwa?
Ngaba kuphosakele ukubulala izilwanyana?
1.244127
Akulu awiri anapita kukamuona.
Abadala ababini bamtyelela.
1.244082
Baibulo limanena kuti: "Kudzakhala kuuka kwa olungama ndi osalungama."
IBhayibhile ithi: "Kuza kubakho uvuko lwamalungisa nabangengomalungisa."
1.244062
Iye alonga pontho: 'Mbwenye cincino ndisadziwa kuti Mulungu anadzakupasani pyonsene pinamphemba imwe.'
Kodwa nangoku ndiyazi ukuba uThixo wokunika nantoni na oyicelayo kuye. ""
1.244041
Choncho musalole kuti Satana akupusitseni.
Ngoko ungaqhathwa nguSathana.
1.243992
39Koma ife sindife amodzi a iwo obwerera mʼmbuyo mwa mantha ndi owonongedwa, koma ndife amodzi a amene akukhulupirira ndi wopulumutsidwa.
Ke thina asingabahlehla baye entshabalalweni; singabokholo olusa ekuzuzeni umphefumlo.
1.243959
Nanga kodi n'zotheka kudzakhaladi m'Paradaiso?'
Ngaba ingaze ibekho nyhani?'
1.243937
Ndani tsopano adzakhala ndi zinthu zonse zimene unazisunga?'
Ngobu busuku uzakufa, Ziyakuba zezikabani ezi zinto uziqokekeleyo?
1.243896
Zomwe anthu adachitazi adayamba kuseka, chifukwa adadziwa kuti mtsikanayo wamwalira.
Kodwa bamwa ngentsini behlekisa ngaye uYesu, kuba besazi ukuba umntwana ufile.
1.243855
Iye ndi Atate wachikondi ndipo ankateteza komanso kusamalira atumiki ake okhulupirika monga Nowa, Abulahamu ndiponso Davide.
Ekubeni enguBawo onothando, ebebakhusela yaye ebanyamekela abakhonzi bakhe abanyanisekileyo abafana noNowa, uAbraham noDavide.
1.243813
Choncho iye anamuitanitsa ndi kumuuza kuti, 'Kodi ndikumva za iwe?
Ngoko wabizela kuye waza wathi kuye, 'Yintoni na le ndiyivayo ngawe?
1.243776
Onse ankadziwa kuti ayenera kupemphera kwa ndani.
Babesazi ukuba kufanelwe kuthandazwe kubani.
1.243726
amene musungidwa ndi mphamvu ya Mulungu mwa chikhulupiriro, kufikira chipulumutso chokonzeka kukavumbulutsidwa nthawi yotsiriza.
nina bathe ngamandla kaThixo ngokholo balondolozelwa elusindisweni, olulungiselwe ukutyhilwa ngexesha lokugqibela.
1.243719
Iye sanali ngati David, kapena inu, kapena ine.
Waye akaba njengoDavide, okanye, okanye mna.
1.243667
Dzichepetseni pamaso pa Ambuye, ndipo Iye adzakukwezani.
Zithobeni phambi kweNkosi, njalo izaliphakamisa.
1.243649
Ndipo adapereka ena akhale atumwi, ena ngati aneneri, ena ngati alaliki, ena ngati abusa ndi aphunzitsi, " (Aefeso 4: 11)
Waza kwayena wabapha abanye ukuba babe ngabapostile, abanye babe ngabaprofeti, abanye babe ngabashumayeli beendaba ezilungileyo, abanye babe ngabalusi nabafundisi,
1.243647
Yezu atsandzaya pidabva iye mphangwa zenezi, mbalonga: 'Ndikuona Sathani agwa kale ninga njazi buluka kudzulu.
Wathi ke kubo: "Ndibone uSathana esiwa ezulwini okombane.
1.243486
pakuti Mzimu Woyera adzaphunzitsa inu nthawi yomweyo zimene muyenera kuzinena.
kuba uMoya oyiNgcwele uya kuthi ngelo xesha anifundise oko manikuthethe."
1.243472
Kampani yathu ali oposa 20 inde ...
Inkampani yethu ngaphezu kwama-20 ewe ...
1.243447
Dziko lapansili silidzawonongedwa ndi moto kapena china chilichonse.
Umhlaba awuzukutshatyalaliswa ngomlilo okanye ngenye indlela.
1.243402
Ndipo dziko silinathe kuwakwanira iwo, kuti akhale pamodzi: chifukwa kuti chuma chawo chinali chambiri, ndipo sanathe kukhala pamodzi.
Ilizwe elo alaba nakubathwala, ukuba bahlale ndawonye; ngokuba impahla yabo yayininzi, ababa nakuhlala ndawonye.
1.243394
"Kenako [Yesu Khristu] anagwira chinjoka, njoka yakale ija, amene ndi Mdyerekezi ndiponso Satana, ndi kumumanga zaka 1,000.
'Wayibamba uYesu Kristu inamba, loo nyoka yantlandlolo, enguMtyholi, uSathana, waza wayibopha iminyaka eliwaka.
1.243366
Lonjezoli liyenera kuti linalimbikitsa Zekariya.
UZekariya umele ukuba womelezwa sesi sithembiso.
1.243345
KODI zinthu zinali bwanji zaka masauzande apitawo?
KWAKUPHILWA njani kumawaka eminyaka eyadlulayo?
1.243327
Sizikutanthauza kuti Mulungu ankayendadi ndi Nowa padziko lapansili kapena Nowa anapita kumwamba n'kumakayenda ndi Mulungu.
Yayingathethi kuthi uThixo wayehamba emhlabeni okanye uNowa yena waya ezulwini.
1.243218
Mulungu ali ndi malo enieni amene amakhala ndipo ndi kumwamba.
UThixo unendawo ahlala kuyo - isezulwini.
1.24319
Iye anati: "Pamene ine ndi mkazi wanga tinkada nkhawa kwambiri, tinkapempha wachibale wina, yemwe ndi mkulu mu mpingo, kuti abwere kudzapemphera nafe.
Uthi: "Sinomkam sasisithi xa kunzima sicele isalamane sethu esingumdala webandla ukuba size kuthandaza nathi.
1.243166
20 - Milandu imene tawina ku Khoti Loona za Ufulu wa Anthu ku Ulaya kuyambira mu April 2000
20 - Amatyala esiye saphumelela kuwo kwiEuropean Court of Human Rights ukususela ngoAprili 2000
1.243152
Koma Nyumba ya Mulungu imene amanena linali thupi lake.
Yena ke wayethetha ngetempile yomzimba wakhe.
1.243147
Anakukonzera zimenezi pa tsiku limene unalengedwa.
Zalungiswa ngemini owadalwa ngayo.
1.243115
Zoipa za tsiku lililonse n'zokwanira pa tsikulo.'
Imini nganye inobayo ububi obuyilingeneyo."
1.243091
Big tech: 'tikufuna thandizo lanu'
Itekhnoloji enkulu: 'sifuna uncedo lwakho'
1.24309
Farao akuuza Yosefe maloto ake: 'Ndinaona ng'ombe zisanu ndi ziwiri zonenepa, zokongola.
UFaro uxelela uYosefu amaphupha akhe: 'Ndibone iimazi zeenkomo ezisixhenxe ezityebileyo, ezintle.
1.243066
Ndipo pomwepo ambiri adzakhumudwa, nadzaperekana wina ndi mzache.
Ngelo xesha baninzi abaya kukhutyekiswa, banikelane, bathiyane.
1.243041
"Palibe Thanthwe Lofanana Ndi Mulungu Wathu"
"Akukho Liwa LinjengoThixo Wethu"
1.242983
Nthaŵi zonse Mulungu wathu sadzataya anthu amene ali okhulupirika kwa iye.
UThixo wethu akasayi kuze nanini na abashiye abo banyanisekileyo kuye.
1.242937
NI NTHAWI ya msonkhano wofunika kwambili m'Yerusalemu.
LIXESHA lentlanganiso ebaluleke kakhulu eYerusalem.
1.242937
Farao ndi antchito ake onse anaona kuti Yosefe wanena zanzeru.
UFaro nabanye abasebenzi bakhe balibona lilelobulumko icebo likaYosefu.
1.242895
Kulambira Koona Kumagwirizanitsa Anthu
Unqulo lokwenyaniso lumanyanisa abantu
1.242878
Koma ife tinamuyankha kuti, "Si nkhosa zanu, ndi nkhosa za Mulungu."
Saphendula sathi, "Ayizozakho, zezikaThixo."
1.242877
Pa tsiku limeneli, Mulungu adzawononga anthu onse oipa.
Ngelo xesha, uThixo uza kubasusa bonke abantu abangendawo.
1.242875
Pakuti iye adzakhala wamkulu pamaso pa Ambuye, ndipo sadzamwa konse vinyo kapena kachasu; nadzadzazidwa ndi Mzimu Woyera, kuyambira asanabadwe.
Kuba uya kuba mkhulu emehlweni eNkosi, angakhe asele wayini nasiselo sinxilisayo; uya kuzaliswa nguMoya oyiNgcwele kwasekuzalweni kwakhe.
1.242858
Ndi chikhulupiriro chimenechi makolo athu akale anayamikidwa.
Kuba amanyange angqinelwa ngokuba nalo olo.
1.242814
"Tiuzeni, Kodi Zinthu Zimenezi Zidzachitika Liti?"
"Sixelele, Ziya Kubakho Nini Na Ezi Zinto?"
1.24281
Mfumu yanzeru Solomo inalemba kuti: "Kanthu kali konse kali ndi nthawi yake."
UKumkani uSolomon owayesisilumko wathi: "Yonke into inexesha layo elimisiweyo."
1.242805
Iwo ayenera kuti anaphunzitsa mwana wawo, dzina lake Samisoni, chilamulo cha Mulungu ndipo zotsatira zake zinali zabwino.
Ngokuqinisekileyo bafundisa unyana wabo, uSamson, umthetho kaThixo yaye imigudu yabo yaphumelela.
1.242784
42Mfumu yayikazi yakummwera idzayimirira pa tsiku lachiweruzo ndi mʼbado uwu ndipo idzawutsutsa pakuti inachokera kumathero a dziko lapansi kudzamva nzeru za Solomoni, ndipo pano pali woposa Solomoni.
Ukumkanikazi welasezantsi uya kusuka eme ngomgwebo nesi sizukulwana, asigwebe; ngokuba wavela eziphelweni zomhlaba, esiza kuva ubulumko bukaSolomon; kanti ke omkhulu kunoSolomon nanku apha.
1.242722
amene anakhala wokhulupirika kwa iye adamuikayo, monganso Mose m'nyumba yace yonse.
Wathembeka kiloyo owamkhethako wambeka njengoMosi owabegade anjalo kiyo yoke indlu kaZimu.
1.24268
Ndatero kuti mudziwe ndithu kuti mawu amene munaphunzitsidwa ngoonadi.
ukuze uyazi kakuhle ingqiniseko yamazwi owafundisiweyo ngomlomo.
1.242669
Popeza wadzichepetsa chifukwa cha ine, sindidzabweretsa tsokali m'masiku ake.
Ngenxa yokuba ezithobile ngenxa yam, andiyi kuyizisa intlekele ngemihla yakhe.
1.242649
Pali chimene chachitika kapena?'" - Masami, Japan.
Ngaba kukho into eyenzekileyo?'" - uMasami waseJapan.
1.242642
Watsegula bwanji maso ako?"
Uwavule njani na amehlo akho?"
1.242561
"Koma khalani akuchita mawu, osati akumva okha, ndi kudzinyenga nokha ndi mabodza.
"Yibani ngabenzi belizwi hayi ngumphulaphuli kuphela, belahlekisa ngokwenu.
1.242494
Iye anayankha kuti, "Ndinaona Satana akugwa kuchokera kumwamba ngati mphenzi.
Wathi ke kubo: "Ndibone uSathana esiwa ezulwini okombane.
1.242454
Tiyeni tisankhe m'tsogoleri watsopano m'malo mwa Mose, ndi kubwerera ku Igupto!'
Masizinyulele inkokeli entsha endaweni kaMoses, size sibuyele eYiputa!'
1.242413
Iwo anati, "Munthu uyu akukopa anthu kuti azipembedza Mulungu mwanjira zotsutsana ndi malamulo athu."
esithi, Lo uzamela ukweyisa abantu ukuba bamhlonele uThixo ngokunxamnye nomthetho.
1.242398
Kodi mungathandize bwanji anthu odwala komanso okalamba?
Ungabasiza njani abantu abagulako nabalupheleko?
1.24237
Zimenezi sizinkandisangalatsa kwenikweni." - James. *
Zange ihle kamnandi kum le nto!" - UJames. *
1.242331
Mwamuna amene akufuna kukwatira ayenera kukonzekera bwino udindo umenewo.
Indoda efuna ukutshata ifanele iyilungele le mbopheleleko.
1.242291
Koma aliyense amene ataya moyo wake, chifukwa cha Ine, ndi chifukwa cha Uthenga Wabwino, adzaupulumutsa.
Osukuba ke eya balahlekelwe ubomi bakhe, ngenxa yam nangenxa yeendaba ezilungileyo, wowusindisa.
1.242279
Mwamuna amene akufuna kukwatira ayenera kukonzekera udindo wake.
Indoda efuna ukutshata ifanele iyilungele le mbopheleleko.
1.242277
Pakuti kumene kuli awiri kapena atatu asonkhanira m'dzina langa, ndiri komweko pakati pao.
Kuba apho bahlanganisene khona egameni lam, nokuba babini nokuba bathathu, ndikho mna apho phakathi kwabo.
1.242273
Choncho kulimbikitsana wina ndi mzake ndi mawu awa.
Ngoko ke thuthuzelanani ngala mazwi.
1.242269
Melbourne, palibe amene amagona usiku uliwonse!
Melbourne, akukho mntu ulala ubusuku ngabunye!
1.242269
Pali kwalembedwa, kuti Abrahmu adali nawo ana amuna awiri, mmodzi mwa mdzakazi, ndi m'modzi mwa mkazi waufulu.
Kuba kubhaliwe kwathiwa, uAbraham wayenoonyana ababini: omnye engowekhobokazana, omnye engowomfazi okhululekileyo.
1.242217
Pakuti iye adzakhala wamkulu pamaso pa Ambuye, ndipo sadzamwa konse vinyo kapena kachasu; nadzadzazidwa ndi Mzimu Woyera, kuyambira asanabadwe.
Yena uya kubaluleka eNkosini, angaseli wayini nasiselo sinxilisayo, alawulwe nguMoya oyiNgcwele kwasekuzalweni kwakhe.
1.242216
2:12 Ichi chidzakhala chizindikiro kwa inu: mudzapeza mwana wakhanda wokutidwa ndi nsalu atagona modyera. "
2:12 Kwaye oku kuya kuba ngumqondiso kuwe: uya kufumana usana lusongelwe eziqhiyeni, lulele emkhumbini wesitali. "
1.242197
pakuti chipatso cha kuunika tichipeza m'ubwino wonse, ndi chilungamo, ndi choonadi,
Kuba sona isiqhamo soMoya sikuko konke ukulunga, nobulungisa, nenyaniso;
1.242196
Poti ndiwe mwana, nthawi zina mwina ungachite mantha kutsatira malamulo a Mulungu.
Njengomntu oselula, maxa wambi usenokoyika ukuthobela imiyalelo kaThixo.
1.24216
6 Sindidzaopa anthu masauzande makumimakumi
6 Andiyi kuwoyika amashumi amawaka abantu
1.242158
'Mverani Ndipo Mumvetse Tanthauzo Lake'
'Phulaphulani Nize Nifumane Intsingiselo'
1.242156
Iwo sanafooke ndipo ankachita zinthu mogwirizana ndi mapemphero awo.
Baqhubeka besenza umzamo kwaye besenza ngokuvumelana nemithandazo yabo.
1.242155
Mwana: Masiku ano sindikufunanso zopita kumisonkhano.
Unyana: Mna andisakufuni ukuya ezintlanganisweni.
1.242154
nsautso ndi kuwawa mtima, kwa moyo wa munthu ali yense wakucita zoipa, kuyambira Myuda, komanso Mhelene;
Kuya kubakho imbandezelo nobunzima kubantu bonke abenza okubi, kumJuda kuqala kwanakowolunye uhlanga ngokunjalo.
1.242128
Pakuti amene Mulungu anawadziwiratu, anawasankhiratunso kuti akonzedwe mʼchifanizo cha Mwana wake, kuti Iye akhale Mwana woyamba kubadwa mwa abale ambiri.
Kaloku abo wayeselebazi kwangaphambili, wabamisela ukuba babe ngumfanekiso woNyana wakhe, ukuze uNyana wakhe abe ngowamazibulo kusapho olukhulu.
1.242108
Musalole kuti munthu akuposeni mphamvu."
Musa ukuvumela umntu ofayo abe namandla nxamnye nawe."
1.242031
M'mawu anuanu, fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.
Ngamazwi akho, chaza oko kwenzekayo kumfanekiso ngamnye.
1.242021
Iye anati: "Chifukwa chake dikirani; chifukwa simudziwa tsiku limene Ambuye wanu adzabwera ...
"Phaphani ngoko, kuba ningàwazi umhla wokufika kweNkosi yenu.
1.241993
Anthu Ofunika Kwambiri Kuwaphunzitsa Baibulo
Ezona Zifundo Zakho ZeBhayibhile Zibalulekileyo
1.241962
Kodi inunso munayamba mwamva ngati mmene Yosefe ankamveramu?
Ngaba wakhe wavakalelwa njengoYosefu?
1.24196
2 Nawonso angelo ndi alaliki.
2 Iingelosi nazo zingabavangeli.
1.241956
Malangizo: Chitani zotsatirazi muli pamalo opanda phokoso.
Imiyalelo: Funda ezi ndinyana zingezantsi kwindawo engenaziphazamiso.
1.241939
Yesu anawawuza kuti, "Atate anga amagwira ntchito nthawi zonse mpaka lero lino, ndipo Inenso ndili pa ntchito."
Wawaphendula ke uYesu wathi, UBawo uyasebenza kude kube ngoku;ndiyasebenza. "