score
float32
1.04
1.25
Chichewa
stringlengths
1
762
Zulu
stringlengths
9
500
1.248304
Kapena ndani anakupatsani ulamuliro umenewu?" - Maliko 11:28.
Namkha ngubani okunikele amandla wokwenza izintwezi?" - Markosi 11:28.
1.248277
Ine mtumiki wanu ndikumva.'
Inceku yakho ilalele.'
1.248271
Koma musaiwale kucitira cokoma ndi kugawira ena; pakuti nsembe zotere Mulunguakondweranazo.
Kepha maningakhohlwa ukwenza okuhle nokuphana, ngokuba iminikelo enjalo uNkulunkulu uthokoziswa yiyo.
1.248265
Pakuti sindinakubisirani pakukulalikirani uphungu wonse wa Mulungu.
Ngokuba angigwemanga ukunitshela lonke icebo likaNkulunkulu.
1.248237
Kumbukirani kuti Mulungu sanaiwale anthu a chiyuda.
Khumbula ukuthi uNkulunkulu akasikhohliwe abantu bamaJuda.
1.248232
Mwachitsanzo, ndi ogula angati
Isibonelo, bangaki abathengi
1.248227
Iye anati: "Ndinapemphera kwa Yehova kuti azinditeteza komanso kuti andithandize kuti ndizim'khulupirira.
Uthi: "Ngathandaza kuJehova ngacela isivikelo sakhe nokuba angisize ngimethembe.
1.248221
14 Pakuti kwadziwikadi kuti Ambuye wathu adatuluka mwa Yuda; za fuko ili Mose sadayankhula kanthu ka ansembe.
14 Kusemtarini bona iKosethu ivela kwaJuda, kodwana uMosi akhenge atjho litho ngokuthi abaphristi bavela ekorweni leyo.
1.248186
Ndipo wow, ndine wokondwa kuti ndinali ndi chisangalalo kumva Andrea akuyankhulanso!
Futhi wow, ngiyajabula ukuthi ngibe nenjabulo yokuzwa u-Andrea ekhuluma futhi!
1.248177
Mawu Ake amatilimbikitsa 'kumufufuza ndi kumupeza, ngakhale sakhala patali ndi yense wa ife.'
IZwi lakhe lisikhuthaza ukuba 'simphumputhe futhi simthole ngempela, nakuba, eqinisweni, engekude kulowo nalowo kithi.'
1.248161
Ndinapita Kiev mwezi watha anzanga.
Ngaya Kiev ngenyanga edlule abangane bami.
1.248117
Mtumwi Yohane analemba kuti: "Pakuti tonsefe tinalandira zinthu kuchokera pa zochuluka zimene ali nazo.
Umpostoli uJwanisi wathi: "Ngokuzala kwakhe umusa saphiwa soke umusa phezu komusa."
1.248113
Kudzera mwa Iye aliyense amene akhulupirira, alungamitsidwa kuchoka ku tchimo lililonse limene silingachoke ndi Malamulo a Mose.
yilowo nalowo okholwayo uyakulungisiswa ngaye.
1.248102
January 2013 _ Kodi Muyenera Kuopa Kutha kwa Dzikoli?
January 2013 _ Ingabe Kufanele Ukwesabe Ukuphela Kwezwe?
1.248081
Komabe anasonyeza kuti anali onyada.
Kodwa babonisa ukuqhosha.
1.24807
Ananena kuti: "Ameneyu adzakhala wamkulu ndipo adzatchedwa Mwana wa Wam'mwambamwamba.
Uyoba mkhulu, futhi uyobizwa ngokuthi iNdodana yoPhezukonke;
1.248069
Ife tikudziwa kuti munthu uyu ndi wochimwa."
Siyazi ukuthi lo muntu uyisoni. "
1.248069
Aliyense amene waona Ine, waonanso Atate.
Ongibonile mina umbonile uBaba.
1.248067
Mwa icinso Mulungu anamkwezetsa iye, nampatsa dzina limene liposa maina onse,
Ngalokho-ke noNkulunkulu wamphakamisa kakhulu, wamnika igama elingaphezu kwawo wonke amagama , ukuze ngegama likaJesu onke amadolo aguqe,
1.248051
"Aliyense amakonda Tacos, sichoncho?
"Wonke umuntu uyawathanda ama-Tacos, akunjalo?
1.248011
Ndipo Manda+ anali kumutsatira pafupi kwambiri.
IThuna belimlandela eduze.
1.247997
Ndipo anati kwa iwo, Ndinaona Satana alinkugwa ngati mphezi wochokera kumwamba.
Wathi kubo: "Ngabona uSathane ewa ezulwini njengonyazi.
1.247994
"Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama. . . .
"Indlela yenu yokuphila mayingabi nalo uthando lwemali . . .
1.247991
Koma musaiwale kuti anthu amene sataya mtima ndi amene adzalandire mphoto.
Kodwa khumbula: Umvuzo uyotholwa yilabo abangakhathali.
1.247988
Mwamunayo adati: 'Ni Msamariya ule.
Indoda leyo yaphendula yathi: 'Yindoda emSamariya.
1.247964
inu ana a Yakobo, osankhika ake.
nina bantwana bakaJakobe, abakhethiweyo bakhe.
1.247959
Yezu apitiriza kulonga: 'Ndzidzi uli kudza, ande wafika, alambiri andimomwene anadzalambira Babanga mu nzimu na mu undimomwene, thangwi iyembo Baba asasaka anyakumulambira ninga anewa.'
UJesu waraga wathi: "Kodwana isikhathi siyeza, begodu sebesifikile, lapha abathandazako bazakuthandaza uBaba ngommoya nangeqiniso ngombana uBaba uthanda abamlotjha njalo."
1.247928
Koma Kim sankachita nawo zimenezi.
UKim wayengenazo izindaba ezinjalo angazixoxa.
1.247924
Mwachitsanzo, Ndimakonda kuvina.
Ngokwesibonelo, Ngiyakuthanda ukudansa.
1.247915
Mulungu analenga anthu awiri, Adamu ndi Hava, ndipo anawauza kuti: "Muberekane, muchuluke, mudzaze dziko lapansi."
UNkulunkulu wadala abantu ababili, u-Adamu no-Eva, wathi kubo: "Zalani nande nigcwalise umhlaba niwunqobe."
1.247913
Ndipo mukakhala mwana wa mtendere m'menemo, mtendere wanu udzapumula pa iye; koma ngati mulibe, udzabwerera kwa inu.
Kuyakuthi uma kukhona lapho indodana yokuthula, ukuthula kwenu kohlala phezu kwayo; kepha uma kungenjalo, kuzakubuyela kini.
1.247907
Ndipo monga momwe tinabadwa ofanana ndi munthu wa dziko lapansi uja, momwemonso tidzakhala ofanana ndi munthu wakumwamba.
49 Njengombana senziwe safana naloyo owenziwe ngethuli, godu sizokufana naloyo ovela ezulwini.
1.247893
Tiyeni tisankhe m'tsogoleri watsopano m'malo mwa Mose, ndi kubwerera ku Igupto!'
Masikhethe umholi omusha esikhundleni sikaMose, sibuyele eGibhithe!'
1.247884
Muyenera kukonda "Weird Al."
Kufanele uthande i- "Weird Al."
1.247855
Iye wandithandiza, moti mtima wanga ukukondwera."
Ngisiziwe, kangangokuba inhliziyo yami iyethaba."
1.247831
pamene adzadza kudzalemekezedwa mwa oyera mtima ake, ndi kukhala wodabwizitsa mwa onse akukhulupirira (popeza munakhulupirira umboni wathu wa kwa inu) m'tsiku lija.
nxa efika ukuba akhazimuliswe kubo abangcwele bakhe, abe ngomangalisayo kubo bonke abakholwa ngalowo muhla, ngokuba nakholwa ngukufakaza kwethu.
1.247717
Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka."
Njengoba ekwesokunene sami, angiyikuzanyazanyiswa."
1.247706
Sikuti ndi Los Angeles kokha. . .
Ayisiyo-Los Angeles nje kuphela. . .
1.247703
Chifukwa mwa kudzala kwake tinalandira ife tonse, chisomo chosinthana ndi chisomo.
Ngokuba ekuzaleni kwakhe sonke samukelwanga, ubabalo lubabalo.
1.247658
Mose ankadziwa tanthauzo la dzina la Mulungu ndipo zimenezi zinalimbitsa chikhulupiriro chake
UMose wayeyazi incazelo yegama likaNkulunkulu futhi lokho kwaluqinisa ukholo lwakhe
1.247621
Kodi iwe susangalala kuti Mulungu anapanga dzuŵa? -
Awujabuli yini ngokuthi uNkulunkulu wenza ilanga? -
1.247617
Pakutinso anadwaladi pafupi imfa; komatu Mulungu anamchitira chifundo; koma si iye yekha, komatu inenso, kuti ndisakhale nacho chisoni chionjezereonjezere.
Ngokuba nempela wayegula ephansi kokufa; kepha uNkulunkulu wamhawukela, kungeyena yedwa, wangihawukela nami, ukuze ngingabi nalusizi phezu kosizi.
1.247547
Mulungu atumiza zilango ziwiri: chimodzi chidzakhala munkhondo, zigawenga, ndi zoyipa zina; lidzachokera kudziko lapansi.
UNkulunkulu uzothumela izijeziso ezimbili: eyodwa izoba sesimweni sezimpi, ukuvukelwa, nobunye ububi; kuyosuka emhlabeni.
1.247541
Yehova ali ndi tonsefe, osati iweyo ndi Aroni basi.'
UJehova uphakathi kwethu sonke, hhayi kuwe no-Aroni kuphela.'
1.247538
Heb 7:14 Pakuti kwadziwikadi kuti Ambuye wathu adatuluka mwa Yuda; za fuko ili Mose sadayankhula kanthu ka ansembe.
14 Kusemtarini bona iKosethu ivela kwaJuda, kodwana uMosi akhenge atjho litho ngokuthi abaphristi bavela ekorweni leyo.
1.247532
Chikondi sichitha nthawi zonse, koma kapena zonenera zidzakhala chabe, kapena malilime adzaleka, kapena nzeru idzakhala chabe.
Uthando (Love) alusoze lwaphela: ko dwa noma ngabe kukhona ukuprofetha kuyakuphela; Nokuba kuyizilimu ziyakunqamuka; nakuba kuyakuba ulwazi luyakukhawuka.
1.247531
Koma ngati ife tiyembekeza chimene tikanalibe, ndiye kuti tikuyembekeza modekha mtima.
Kodwa uma sithemba lokho esingakuboniyo, siyakulindela ngokubekezela.
1.247524
Mulungu anaweruza opandukawo chifukwa cha zimene anachitazo.
UNkulunkulu wazahlulela lezi zihlubuki ngenxa yezenzo zazo.
1.247518
Koma iye anayankha, nati kwa iwo, Amai wanga ndi abale anga ndiwo amene akumva mau a Mulungu, nawacita.
Kepha waphendula, wathi kubo: "Umame nabafowethu yilabo abalizwa izwi likaNkulunkulu, balenze."
1.247508
36 Ndipo Simoni ndi amzake adali naye, adamtsata Iye.
36 USimon nalabo ababe naye, bamlandela;
1.247502
Sankangomuona ngati mwana wake chabe, koma ankamuonanso monga Mbuye ndi Mpulumutsi wake.
Khenge amqale njengendodanakhe kwaphela kodwana njengeKosi noMsindisakhe.
1.247489
Ine anandiuza kuti ndidzapita ku Paraguay.
Mina ngatshelwa ukuthi ngizakuya eParaguay.
1.247411
Muli ndi msonkhano mphindi 15?
Unomhlangano emizuzwini engu-15?
1.2474
Iwo ayenera kuti anaphunzitsa mwana wawo, dzina lake Samisoni, chilamulo cha Mulungu ndipo zotsatira zake zinali zabwino.
Kusobala ukuthi bayifundisa indodana yabo, uSamsoni, umthetho kaNkulunkulu, kuyacaca nokuthi imizamo yabo yaphumelela.
1.247388
Ndipo pamene zonsezo: zagonjetsedwa kwa iye, pomwepo Mwana yemwe adzagonjetsedwa kwa iye amene anamgonjetsera zinthuzonse; kuti Mulungu akhale zonse mu zonse.
Kodwa nxa izinto zonke sezithotshiselwe phansi kwakhe, lapho-ke nayo iNdodana iyakuzithoba phansi kwalowo owathobisa zonke izinto phansi kwayo, ukuze uNkulunkulu abe yikho konke kukho konke.
1.247385
Atumiki anga adzasangalala, koma inuyo mudzachita manyazi.
Izinceku zami zizathokoza, kodwa lina lizayangiswa.
1.247374
Ine ndikuwuzani kuti wamkulu kuposa Nyumba ya Mulunguyo ali pano.
Ngiyakutshela lowo mkhulu kune- ithempeli lilapha.
1.247369
Mulungu akutinso, "Ambuye, pachiyambi Inu munayika maziko a dziko lapansi; ndipo zakumwambako ndi ntchito za manja anu.
10 Lokuthi: Wena Nkosi, ekuqaleni wasekela umhlaba, lamazulu ayimisebenzi yezandla zakho;
1.247365
Ndidziwa ntchito zako, ndi chikondi, ndi chikhulupiriro, ndi utumiki, ndi chipiriro chako, ndi kuti ntchito zako zotsiriza zichuluka koposa zoyambazo.
Ngiyayazi imisebenzi yakho, nothando, nokukholwa, nokukhonza, nokubekezela kwakho, nokuthi imisebenzi yakho yokugcina miningi kuneyokuqala.
1.247364
Izi ndi zomwe mumandiwonetsa... ndipo inde, ndakonzeka!
Yilokhu ongikhombisa khona... futhi yebo, ngilungele!
1.247361
Yosefe analota maloto awiri.
UJosefa waba namaphupho amabili.
1.247342
Izi zili pakati pawo ndi Mulungu wawo.
Lokho kuphakathi kwabo noNkulunkulu wabo.
1.247325
Zikutanthauzanso kulambira mogwirizana ndi choonadi; kudziŵa molondola zomwe zili m'Mawu a Mulungu.
Kusho nokukhulekela ngokuvumelana neqiniso, ulwazi olunembile olutholakala eZwini likaNkulunkulu.
1.247323
Mutha kumvera Marko ndi Daniel...
Ungalalela uMarko noDaniel...
1.247321
Ndinaphunziranso kusunga ndalama."
Ngafunda nokubeka imali."
1.247271
"Mike, ndili ndi chakudya chatsopano chokhudza MY SOLAR.
"Mike, nginokudla okusha mayelana ne-MY SOLAR.
1.247252
Choncho Mulungu anamulanga ndi matenda oopsa akhate.
Ngakho uNkulunkulu wamshaya ngochoko, isifo esibi.
1.247211
9 Kodi munachitapo zinthu zimene panopa mumanong'oneza nazo bondo?
9 Ingabe uye wenza izinto ozisola ngazo manje?
1.247197
Koma Iye adati kwa iwo, 24 Yesetsani kulowa chipata chopapatiza; chifukwa anthu ambiri, ndikuwuzani, adzafunafuna kulowamo, koma sadzakhoza.
Wathi kibo: 24 "Sebenzani budisi bona ningene ngomnyango omncani, ngombana ngiyanitjela ukuthi, abanengi bazokufuna ukungena kodwana angekhe bakghone.
1.247191
Kodi panopa simuli ndi ufulu woposa umene munali nawo muli mwana?
Awunayo yini manje inkululeko ethe xaxa kunangesikhathi usemncane?
1.247185
Amen, Amen, ndinena kwa inu: Chilichonse mukapempha Atate m'dzina langa, adzakupatsani inu ."
Amen, Amen, ngithi kini: Noma yini eniyakukucela kuBaba egameni lami, uyokunika ."
1.247181
Onani, kumapeto kwa tsiku, kuli ngati bizinesi.
Bheka, ekugcineni kosuku, kufana nebhizinisi.
1.24718
Kodi mtumwi Paulo ankatanthauza chiyani ponena kuti: "Pamene ndili wofooka, m'pamene ndimakhala wamphamvu"?
Wayesitshoni uPhawuli lapho esithi "nxa ngibuthakathaka, kulapho-ke ngilamandla"?
1.247165
Komabe, Natalie amandithandiza kwambiri.
Noma kunjalo, uNatalie akeve engisekela.
1.24715
Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!
Sengathi nga ulalele imiyalo yami!
1.247121
KODI zinthu zinali bwanji zaka masauzande apitawo?
KWAKUNJANI ukuphila eminyakeni eyizinkulungwane edlule?
1.247121
Mayi Phiri: Ee, ndinaphunzirapo nkhani imeneyi ku Sande Sukulu.
UZandile: Yebo, leyo ndaba ngafunda ngayo kuSonto-sikole.
1.247113
Ndipo, chofunika kwambiri, ndikufuna ndikuthokoze mkazi wanga Amanda.
Futhi, okubaluleke kakhulu, ngifuna ukubonga umkami u-Amanda.
1.247111
Chimodzimodzi inunso, mukachita zonse zimene munapatsidwa ngati ntchito yanu, muzinena kuti, 'Ife ndife akapolo opanda pake.
Kunjalo nani, nxa nikwenzile konke enikuyaliweyo, anothi: 'Asizinceku zalutho; sikwenzile nje ebesifanele ukukwenza.' "
1.247104
Koma kaya mukufuna kuchita chiyani potumikira Mulungu, mufunikabe kukhala ndi njira yopezera zofunika pa moyo.
Kungakhathaliseki ukuthi uyini umgomo wakho enkonzweni kaNkulunkulu, uzoyidinga indlela yokuziphilisa.
1.247089
Mofanana ndi zimene atumwi ankachita, ifenso timalalikira kunyumba ndi nyumba.
Njengabapostoli, sitjhumayela emzini ngomuzi.
1.247065
Kapena atamupempha nsomba, kodi angamupatse njoka?
noma icela inhlanzi, ayinike inyoka na?
1.24706
Ndikukumbukira... anali masiku 10 apitawo.
Ngiyakhumbula... bekuyizinsuku eziyi-10 ezedlule.
1.247045
Pakuti Mose walemba kuti munthu amene achita chilungamo cha m'lamulo, adzakhala nacho ndi moyo.
Ngokuba uMose uloba ukuthi umuntu owenza ukulunga okuvela emthethweni uyakuphila ngakho.
1.247034
Zonse zokhudza Pakistan.
Konke mayelana nePakistan.
1.247011
Ndani angapite ku Europe ndi UK?
Ngubani ongaya eYurophu nase-UK?
1.246997
Odala ndi amene ali oyera mtima, chifukwa adzaona Mulungu.
Babusisiwe abamhlophe ngenhliziyo; ngoba bona bazabona uNkulunkulu.
1.246979
Inakwiya naye kapolo wosakhululukira mnzakeyo.
Yayisiyithukuthelela kakhulu le nceku engaxoleli.
1.246956
Ena a inu mukudziwa ndinkakhala kumpoto Sweden zaka 23 za moyo wanga.
Abanye benu bazi Ngahlala enyakatho yeSweden iminyaka engu-23 yokuphila kwami.
1.24695
Kodi ndi liti pamene kugwirizana kudzakhala kofunika kwambiri?
Kunini lapho ubunye buyobaluleka nakakhulu khona?
1.246939
Ndiponso 'itanani akulu a mpingo [kuti akuthandizeni].'
Futhi, '[cela usizo] emadodeni amadala ebandla.'
1.246937
Koma ngati munthu sadziwa kuweruza nyumba ya iye yekha, adzasunga bwanji Mpingo wa Mulungu?
kepha uma umuntu engakwazi ukuphatha owakhe umuzi, angaliphatha kanjani ibandla likaNkulunkulu na? -
1.246929
Koma musaiwale kucitira cokoma ndi kugawira ena; pakuti nsembe zotere Mulunguakondweranazo.
Ningakohlwa ukwenza okulungileyo nokupana; ngokuba uNkulunkulu uyayitanda kakulu imihlatshelo enjalo.
1.246929
Lonjezani kuti simudzamenyana nafe."
Sithembiseni ukuthi ngeke nilwe nathi."
1.246908
Kodi Satana amachita chiyani kuti zinthu za m'dzikoli zizioneka zabwino?
USathane ulenza kanjani leli zwe ukuba libonakale likhanga?
1.246901
Mwana wa Munthu adzabwera mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo ake, ndipo pomwepo mphoto kwa munthu aliyense monga mwa ntchito zake.
Ngokuba iNdodana yomuntu iyakuza ngenkazimulo kaYise kanye nezingelosi zayo; khona-ke iyakuvuza yilowo nalowo ngesenzo sakhe.
1.246896
Ndipo Paulo ananyamuka, nakodola ndi dzanja, nati, Amuna a Israyeli, ndi inu akuopa Mulungu, mverani.
Wayesesukuma uPawulu, waqhweba ngesandla, wathi: "Madoda akwa-Israyeli, nani enesaba uNkulunkulu, lalelani:
1.246865
'Dzipulumutseni Nokha ndi Iwo Akumva Inu'
'Zisindise Wena Nabakulalelayo'
1.246862
Koma ndani anatiphunzitsa choonadi? '
Kodwa ngubani owasifundisa iqiniso? '
1.246839
Mulungu anasintha n'kulolera zimene Loti anapempha.
UNkulunkulu wasamukela isicelo sikaLoti.