score
float32
1.04
1.25
Chichewa
stringlengths
1
762
Zulu
stringlengths
9
500
1.249993
Ndikukupemphererani kuti mudziwe chikondi chija cha Khristu chopitirira nzeru za anthu, kuti mudzazidwe kwathunthu ndi moyo wa Mulungu mwini.
nokulwazi uthando lukaKristu oludlula ukwazi konke, ukuze nigcwaliswe kube ngukugcwala konke kukaNkulunkulu.
1.249943
Ena mwa anthu anu adzapulumuka, iwo amene alembedwa m'buku.
Abanye abantu bakho bazophunyuka, labo ababhalwe phansi encwadini.
1.249915
Ndimakonda Japan, kotero kuti ndakhala ndikupita kutchuthi atatu atatu apitawa.
Ngiyayithanda iJapan, kangangoba ngiye eholidini kulezi ezintathu zokugcina.
1.24989
Kaya ankaganiza zotani, kuganizira malangizo amene Mulungu anamupatsa kukanamuthandiza.
Kungakhathaliseki ukuthi wayecabangani, wayengakhumbula isiyalo sikaNkulunkulu.
1.249888
Komanso, dzanja la Yehova linali nawo, ndipo ambiri anakhulupirira natembenukira kwa Ambuye.
Ngaphezu kwalokho, isandla sikaJehova sasinabo, futhi inani elikhulu laba ngamakholwa laphendukela eNkosini.
1.249878
Ambiri mwa atumiki a moto Mulungu.
Iningi umlilo izigqili kuNkulunkulu.
1.24986
(Gen. 5:2) Pa nthawi yake yoyenerera, Mulungu adzawononga angelo oipawa.
(Gen. 5:2) Iingilozi ezimbi nezingalalelikwezi zizokutjhatjalaliswa ngesikhathi esibekwe nguZimu.
1.249837
Ndikuganiza kuti inali Facebook.
Ngicabanga ukuthi bekuyi-Facebook.
1.249832
Ngati anazunza ine, inunso adzakuzunzani."
Uma beye bashushisa mina, bayonishushisa nani."
1.249821
Mfumukazi ya Indies ndi Mgonjetsi - Kuyambira Meyi 16
INdlovukazi yama-Indies kanye noMnqobi - Kusukela ngoMeyi 16
1.249798
Munganene kuti: "Ndinapeza lemba lolimbikitsa kwambiri ili."
Ungase uthi: "Uyazi ngithole nanku umbhalo okhuthazayo."
1.249777
Nthaŵi zina anali kufuna kukhala payekha polankhula ndi Mulungu.
Ngezinye izikhathi wayethanda ukuba yedwa lapho ekhuluma noNkulunkulu.
1.249748
Kodi muli ndi abwenzi angati pa Facebook?.
Unabangane abangaki ku-Facebook?.
1.249736
Munthu wolungama Elihu anati: "N'kutali ndi Mulungu kuchita choipa, ndi Wamphamvuyonse kuchita chosalungama."
U-Elihu othembekile wathi: "Makube kude noNkulunkulu weqiniso ukwenza ngendlela yokukhohlakala, noMninimandla onke ukwenza ngokungabi nabulungisa!"
1.249697
Inu muli nawo mawu a moyo wosatha."
Nguwe onamezwi wokuphila okungapheliko."
1.249692
Kwa zaka 17 ndinkapemphera kuti ndipeze mayankho a mafunso anga.
Ngathandaza iminyaka engu-17 ukuze ngithole izimpendulo zemibuzo yami.
1.249687
Ndipo ndili nanu pakhungu langa.
Futhi nginawe esikhunjeni sami.
1.249637
Ngakhale anthu amene amapita kutchalitchi sadziwa bwinobwino Malemba.
Ngisho nabaningi abathi bayasonta banolwazi oluncane lwemiBhalo.
1.249634
Kodi mtumwi Paulo ankatanthauza chiyani ponena kuti: "Pamene ndili wofooka, m'pamene ndimakhala wamphamvu"?
Umphostoli uPawulu wayesho ukuthi lapho ebhala ukuthi: "Lapho ngibuthakathaka, kulapho-ke nginamandla"?
1.249628
Chifukwa ndimakukondani, ndikufuna kukuwonetsani zomwe ndikuchita mdziko lapansi lero.
Ngoba ngiyakuthanda, ngifuna ukukukhombisa engikwenzayo emhlabeni namuhla.
1.249624
iwo anaona ophunzira ake akudya chakudya ndi mʼmanja mwakuda kapena kuti mʼmanja mosasamba.
Sebebonile ukuthi abanye babafundi bakhe badla izinkwa ngezandla ezimbi okungukuthi ezingahlanjiwe -
1.249598
Koma munthu akayenda usiku, amapunthwa pa chinachake chifukwa mwa iye mulibe kuwala."
Kodwa uma umuntu ehamba ebusuku, uyakhubeka, ngoba ukukhanya akukho kuye."
1.249565
Ndimagwirizana ndi inu kuti Mulungu 100% zabwino.
Ngivumelana nawe ukuthi uNkulunkulu 100% okuhle.
1.249563
20 Kodi tingakhale tani na cikhulupiro ninga ca Djobi?
20 Indlela esingaluhlakulela ngayo ukholo olufana nolukaJobe.
1.249502
Lero ndi tsiku loyamba la moyo wanu wonse, Calvin.
Namhlanje usuku lokuqala of the impilo yakho yonke, Calvin.
1.249498
Ndipo nenani kwa Arkipo, Samaliratu utumiki umene udaulandira mwa Ambuye, kuti uukwanitse.
Nimtshele u-Arkiphu, nithi: "Qaphela inkonzo oyitholile eNkosini, ukuze uyifeze."
1.249495
Ukatumikira milungu yawo, umenewo udzakhala msampha kwa iwe."+
Uma kwenzeka ukhonza onkulunkulu babo, kuyoba ugibe kuwe."+
1.249484
amene kale sanakupindulira, koma tsopano watipindulira bwino iwe ndi ine;
okade engenalusizo kuwe, kepha kalokhu unosizo nakuwe nakimi,
1.249482
Pakuti aliyense wokhala ngati wamng'ono pakati pa nonsenu ndi amene ali wamkulu."
Ngoba lowo oziphatha njengomncane phakathi kwenu nonke nguye omkhulu."
1.249459
Zimenezi nʼzofanizira chabe, ndipo zinkalozera nthawi ino, kusonyeza kuti mphatso ndi nsembe zimene zinkaperekedwa sizinkachotsa chikumbumtima cha wopembedzayo.
elona lingumfanekiso kulesi sikhathi samanje, okulethwa ngawo iminikelo nemihlatshelo engenakumenza okhonzayo aphelele maqondana nonembeza,
1.249451
Ngati anazunza ine, adzakuzunzani inunso."
Uma beye bashushisa mina, bayonishushisa nani."
1.249411
Izi ndi zimene mayi wina wa ku Japan ankachita pophunzitsa ana ake awiri.
Kunomma weJapan owakwenzako lokho.
1.249388
Pakuti Iye amene Mulungu anamtuma alankhula mau a Mulungu; pakuti sapatsa Mzimu ndi muyeso.
Ngokuba lowo uNkulunkulu amthumileyo ukhuluma amazwi kaNkulunkulu; ngokuba akaniki uMoya ngokulinganisela.
1.249344
Kodi ndani amene analenga zinthu zimenezo? . . .
Ngubani odale lezi zinto? . . .
1.249324
Iye adzalanga amene sadziwa Mulungu ndi amene samvera Uthenga Wabwino wa Ambuye athu Yesu.
elangabini lomlilo, ephindisela kwabangamazi uNkulunkulu nakwabangalaleli ivangeli leNkosi yethu uJesu,
1.249266
Uwalamule kuti azichita zabwino, kuti azikhala olemera pa ntchito zabwino, owolowamanja ndi okonda kugawana zinthu zawo ndi anzawo.
Bayale benze okuhle, banothe ngemisebenzi emihle; baphane babele abanye.
1.249259
Ngati munthu ali yense afuna kucita cifuniro cace, adzazindikira za ciphunzitsoco, ngati cicokera kwa Mulungu, kapena ndilankhula zocokera kwa Ine ndekha.
Nanyana ngubani ofisa ukwenza intando yakhe, uzokwazi ukuthi engikufundisako kuvela kuZimu namkha ngikhuluma okuvela kimi."
1.249258
Yesu anayankha nati kwa iwo, Ndinacita nchito imodzi, ndipo muzizwa monse,
UJesu waphendula wathi kubo: Ngenze umsebenzi owodwa, njalo lonke liyamangala.
1.249258
Mose sanachite mantha ndi zimene Farao angachite atamva zimenezi.
UMose wayengesabi.
1.249257
"Futukulani mtima wanu." - 2 Akor.
"Zivuleni ngokupheleleyo izinhliziyo zenu." - 2 Khor.
1.249247
Mbuzi kaya iweyo, maina aja adatulutsidwa aja iweyo sudayaone?
Abahlambalazi igama elihle enibizwa ngalo na?
1.24924
• Kodi ena afeŵetsa zinthu m'moyo wawo m'mbali ziti?
• Yiziphi izici abanye abaye benza ukuphila kwabo kwaba lula kuzo?
1.249207
Komabe iye ankalambiranso Mulungu limodzi ndi banja lake.
Kodwa wayebuye amkhulekele nomndeni wakhe.
1.2492
Kenako ananena kuti: "Ntchitoyi si ya munthu."
Waphinda wathi: "Lo akusimsebenzi womuntu."
1.249148
Yesu anayankha kuti, "Nthawi yafika yakuti Mwana wa Munthu alemekezedwe.
UJesu waphendula, wathi kubo: "Sesifikile isikhathi sokuba ikhazimuliswe iNdodana yomuntu.
1.249116
Ngati masabata angapo apitawa tidayankhula za Hong Kong ndi ...
Uma emasontweni ambalwa edlule sikhulume ngeHong Kong kanye ne ...
1.249077
Pa nthawi imeneyo ambiri adzasiya chikhulupiriro ndipo adzadana ndi kuperekana wina ndi mnzake,
Njalo ngalesosikhathi abanengi bazakhubeka, banikelane, bazondane.
1.249068
(Miyambo 16:24) Muziwapempha kuti akupatseni malangizo ena amene angakuthandizeni kuti muzilera bwino anawo ndipo muziwathokoza akakupatsani malangizowo.
(IzAga 16:24) Cela iseluleko sakhe futhi umbonge lapho ekunika.
1.249066
Paulo anali kudziŵa chifukwa chake anthu anali kumuzunza
UPawulu wayeqonda ukuthi kungani ayeshushiswa
1.249058
Monga bambo ake adachitira, David Moyes nayenso anamutcha mwana wake (David Moyes Jnr).
Njengoba nje ubaba wakhe enza, uDavid Moyes naye wabiza indodana yakhe (uDavid Moyes Jnr).
1.249028
Mtumwi Yohane analemba kuti: "Pakuti tonsefe tinalandira zinthu kuchokera pa zochuluka zimene ali nazo.
Umphostoli uJohane wabhala wathi: "Ngenxa yokugcwala komusa wakhe sonke sizamukele izibusiso ngezibusiso."
1.249026
ndi m'chinyengo chonse cha chosalungama kwa iwo akuonongeka, popeza chikondi cha choonadi sanachilandira, kuti akapulumutsidwe iwo.
nangayo yonke inkohliso yokungalungi kwababhubhayo, ngenxa yokuba bengavumanga ukuthanda iqiniso, ukuze basindiswe.
1.249022
Iye anakopa Ayuda ambiri komanso anthu a mitundu ina.
Wadonsela kuye kokubili amaJuda amaningi kanye nabeZizwe abaningi.
1.249022
Mwina sindikudziwa zambiri za sp ...
Mhlawumbe angazi okuningi nge-sp ...
1.249018
Koma kumbukira kuti tingapemphere kwa Mulungu nthaŵi iliyonse masana kapena usiku, ndipo iye adzatimva.
Kodwa khumbula, singathandaza kuNkulunkulu noma nini emini noma ebusuku, futhi uyosizwa.
1.248984
Iye sanali ngati David, kapena inu, kapena ine.
Wayengafani David, noma wena, noma mina.
1.248984
Wokondedwa, ndiwe wokhulupirika pa zimene ukuchitira abale, ngakhale kuti iwowo ndi alendo.
Sithandwa, wenza okuthembekileyo ngalokho okwenzele abazalwane nokuba bengabafo
1.248966
8 "Kudzachitika zivomezi zamphamvu."
8 "Kuyoba khona ukuzamazama okukhulu komhlaba."
1.248951
20 - Milandu imene tawina ku Khoti Loona za Ufulu wa Anthu ku Ulaya kuyambira mu April 2000
20 - Amacala anqotshwa eNkantolo YaseYurophu Yamalungelo Abantu kusukela ngo-April 2000
1.248947
Ndikufuna ndidzaone mmene azidzachitira zinthu akadzakhala wangwiro."
Ngifuna ukumazi lapho esephelele."
1.248938
6 Mitsonkhano imbatilimbisa.
6 Imihlangano iyasikhuthaza.
1.248911
Cidzindikiro cinafuna kudza kaona imwe ndi ici: Munagumana mwana wa kumala kumbulunganyiwa na nguwo, mbagoneswa m'mwadiya wakudyera pifuyo."
Njalo lokhu kuzakuba yisibonakaliso kini: Lizathola usane lugoqelwe ngamalembu, lulele emkolweni.
1.24889
Ndipo sanathe kuilaka nzeru ndi Mzimu amene analankhula naye.
kepha babengenamandla okumelana nokuhlakanipha noMoya ayekhuluma ngakho.
1.248875
Pakutinso anadwaladi pafupi imfa; komatu Mulungu anamcitira cifundo; koma si iye yekha, komatu inenso, kuti ndisakhale naco cisoni cionjezere-onjezere.
Ngokuba nempela wayegula ephansi kokufa; kepha uNkulunkulu wamhawukela, kungeyena yedwa, wangihawukela nami, ukuze ngingabi nalusizi phezu kosizi.
1.248792
Chifukwa chiyani Purezidenti Trump yekha ndi amene angapulumutse Hawaii tsopano?
Kungani kunguMongameli Trump kuphela ongasindisa iHawaii manje?
1.248784
"Mudzaonanso kusiyana pakati pa munthu wolungama ndi woipa." - MAL.
'Niyowubona umehluko phakathi kolungileyo nomubi.' - MAL.
1.24876
Musaope: Gulu Lankhondo Lonse lakumwamba likuyembekezera
Ungesabi: wonke amabutho asezulwini alindile
1.248749
Anafika podziona ngati anali wolungama kuposa Mulungu.
Wathi yena ulungile kunokuthi athi uZimu ulungile.
1.248737
Iwo apanga nkazi: 'Ife nee tisakhulupira thangwi ya pidalonga iwe basi; ife tabva tekhene, pontho tisadziwa kuti mwandimomwene munthu uyu ndi mpulumusi wa dziko.'
Bathi emfazini: "Asisakholwa ngebanga lalokho ositjele khona kwaphela; ngombana nathi sizizwele ngezethu, begodu siyazi ukuthi umuntu lo kwamambala umsindisi wephasi."
1.248708
Adzabadwa mwatsopano ngati ana aamuna a Mulungu, monga Adamu, pamene analengedwa ngati mwana [wamwamuna] wangwiro wa Mulungu.
Bazophinde bazalwe njengamadodana kaNkulunkulu [aphelele], njengo-Adamu, lapho edalwa njengendodana kaNkulunkulu [ephelele] yomuntu.
1.248694
Baibulo limanenanso kuti madalitso ndiponso chitetezo zimachokera kuphiri la Mulungu.
Godu, iimbusiso nesivikelo zihlobaniswa nentaba kaZimu.
1.248669
Iye adati: 'Iwo ankudziwa lini bzomwe ankucita.'
Wathi: "Nizabazi ngabakwenzako.
1.248664
Injini ikhoza kutembenuzidwa, kotero ine ndinafunsa
Injini ingaphenduka, ngakho ngabuza
1.248658
Anthu anadziŵa kuti Mulungu walankhula, komatu iwo anachita mantha kwambiri.
Abantu babazi ukuthi bekukhuluma uNkulunkulu, kodwa babesaba kakhulu.
1.248657
Atumwiwo anati kwa Ambuye, "Kulitsani chikhulupiriro chathu!"
Abaphostoli base bethi eNkosini: "Yandisa ukukholwa kwethu."
1.248645
KODI pali munthu wodwala amene ukumudziŵa? - Nthaŵi zina nawenso umadwala.
UKHONA yini umuntu omaziyo ogulayo? - Mhlawumbe nawe uye ugule ngezinye izikhathi.
1.24862
Koma Mose ankadziwa kuti Mulungu angasinthe zinthu.
Nokho, uMosi bekazi ukuthi uZimu angayijika yoke intweleyo.
1.248615
Ali ndi ana asanu - Jessica [...]
Unabantwana abahlanu - uJessica [...]
1.248552
Kodi iyenera kuyendetsedwa m'nyumba, kapena mukufunafuna chinachake chachikulu ku thambo lotseguka?
Ingabe kufanele iqhume ngaphakathi endlini, noma ufuna into enkulu ebhakabhakeni evulekile?
1.248548
Kenako mneneriyu anayamba kupemphera kuti: "Inu Yehova, m'tseguleni maso chonde kuti aone."
Umprofethi wabe esethandaza: "O Jehova, ngicela uvule amehlo akhe, ukuze abone."
1.248547
Akhristu ayeneranso kupitiriza kukula
NamaKristu kufanele aqhubeke ekhula
1.248541
Koma pa phiri la Ziyoni padzakhala chipulumutso, ndipo kudzakhala chiyero; ndipo nyumba ya Yakobo idzatenga chuma chawo.
Kepha entabeni yaseSiyoni kuyakuba khona abasindayo, ibe ngcwele, nendlu yakwaJakobe iyakudla ifa layo.
1.248521
Palibe dziko la EU lomwe lingathe kapena liyenera kusiyidwa lokha
Alikho izwe le-EU elingashiya noma okufanele lishiywe lodwa kulo
1.248468
Ndipo ndani adzaime chilili iye akadzaonekera?
Ngubani oyakuma ekubonakaleni kwaso na?
1.248467
Iwo onse adamwalira m'chikhulupiriro, osalandira malonjezano, komatu adawaona ndi kuwalankhula kutali, navomereza kuti ali alendo ndi ogonera padziko.
13 Ngokukholwa boke laba bafa, ngitjho nanyana bangakhenge bafumane ukuzaliseka kweenthembiso; kodwana bazibona zisesekude, bazamukela begodu bavuma tjhatjhalazi ukuthi babaqhamuka nezakhamuzi zesikhatjhana enarheni.
1.248466
Koma ife tikudikira kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano, zimene Mulungu analonjeza, mʼmene chilungamo chidzakhalamo.
Kepha siyalindela ngesithembiso sakhe amazulu amasha nomhlaba omusha okukhona kuwo ukulunga.
1.248462
Pakuti Mulungu anasandutsa anthu onse a mʼndende ya kusamvera kuti Iye akaonetse chifundo kwa onse.
Ngokuba uNkulunkulu ubavalele bonke ekungalalelini ukuze abahawukele bonke.
1.248455
Kenako iye anawauza kuti: "Ndili ndi zambiri zakuti ndikuuzeni, koma simungathe kuzimvetsa zonsezo pakali pano.
UJesu uraga uthi: "Ngisesenezinto ezinengi ekufuze nginitjele zona, kodwana angekhe nikghone ukuzithwala nje."
1.248433
M'malo mwake chitetezo / chitsimikiziro kuti adzalandira cholowa, chifukwa Mulungu anali kuchisunga.
Esikhundleni salokho ukuphepha / isiqinisekiso sokuthi bazothola ifa, ngoba uNkulunkulu wayeyilonda.
1.248432
Kodi iweyo unayamba wanama? - * Ngakhale akuluakulu ena amene amakonda Mulungu ananamapo.
Wake wawaqamba yini wena amanga? - * Ngisho nabantu abadala abathanda uNkulunkulu bake bawaqamba amanga.
1.248406
Iye ankawatsogolera ndi mtambo ndi moto.
Babeqondiswa insika yefu neyomlilo.
1.248401
Kumbukilani atsogoleri anu, amene analankhula nanu Mau a Mulungu; ndipo poyang'anira citsiriziro ca mayendedwe ao mutsanze cikhulupiriro cao.
Bakhumbuleni ababenihola bekhuluma izwi likaNkulunkulu kini, niqonda ukuphela kokuhamba kwabo, nilingise ukukholwa kwabo.
1.248401
Ife tasiya zinthu zonse ndi kukutsatirani, kodi tidzapeza chiyani?"
Sishiyé zonke izinto sakulandela; siyotholani ngempela?"
1.248383
Tsopano ndikondwera, sikuti mwangomvedwa cisoni, koma kuti mwamvetsedwa cisoni ku kutembenuka mtima; pakuti munamvetsedwa cisoni ca kwa Mulungu, kuti tisakusowetseni m'kanthu kali konse.
manje ngiyathokoza, kungengokuba nadabukiswa, kodwa ngokuba nadabukiswa kwaba ngukuphenduka; ngokuba nadabukiswa ngokukaNkulunkulu, ukuze ningalahlekelwa lutho ngathi.
1.248378
Tikhale Oyera M'makhalidwe Athu Onse
Kumelwe Sibe Ngcwele Kukho Konke Ukuziphatha Kwethu
1.248368
Ayi, ndipo nayenso Yobu sanaganize choncho.
Cha, akunjalo, noJobe akacabanganga kanjalo.
1.248367
Ndipo m'mene anthu a makamu anaciona, anaopa, nalemekeza Mulungu, wakupatsa anthu mphamvu yotere.
Kepha izixuku zikubona zethuka, zamdumisa uNkulunkulu onikile abantu amandla anjalo.
1.248343
anthu 10,000 kudzanja lako lamanja,
nabayizinkulungwane eziyishumi ngakwesokunene sakho,
1.24833
Ndipo wokhala pampando wachifumu anati: 'Taonani!
Lowo ohlezi esihlalweni sobukhosi wathi: 'Bheka!
1.248306
Cifukwa cace iye wotaya ici, sataya munthu, komatu Mulungu, wakupatsa Mzimu wace Woyera kwa inu.
Ngakho-ke owalayo akali umuntu, kepha wala uNkulunkulu, yena oninika uMoya wakhe oNgcwele.